Music Video
Music Video
Credits
PERFORMING ARTISTS
Dan Lu
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Dan Lu
Songwriter
Lyrics
Sinkhumbira khala mansion
Sindikhumbila nkhala motoka
Sindikhumbira khalam\'banja
Nkaganiza za imfa
Chinkazichi azachitengewina
Anawa azaalere wina
Ati kwanga kwatha Imfa sizinthu
Katundu wanga azagawane
Munda wanga adzakolore
Thukuta lokhetsa ndekha
Ndagwamphwayi
Ukandiona ndabalalika
Ayi sibawa Ayi si mogo maganizo
Imfa iwe mama
Oh mamane mama
Ndavula chipewa mama mama
Zindalama ku bank nzazisiya
Kutchuka konseku nzakusiya
Maudindo onsewa nzawasiya eeeh
nzawasiya oooh nzawasiya
Ma degree onsewa
Kunanala konseku
Nzazisiyaaa nzazisiya eeeh
Nzawasiya oooh nzazisiya
Ndiodala onyema komwe alinako kooo
Azindikila vyonse ndizotsala
Mukasiketi muja simungakhale sofa
Mukasiketi muja simungakhale kudya
Mukasiketi muja simungakhale kunjoya
Mukasiketi muja
Imfa iwe mama
Oh mamane mama
Ukandiona ndabalalika
Ayi sibawa ayi si mogo maganizo
Zindalama ku bank nzazisiya
Kutchuka konseku nzakusiya
Maudindo onsewa nzawasiya eeeh
Nzawasiya oooh nzawasiya
Ma degree onsewa aaah
Kunanala konseku
Nzazisiyaaaa nzazisiya eeeh
Nzazisiya eeeh nzawasiya
Written by: Dan Lu