Dari
COMPOSITION & LYRICS
Happy Bakolo
Songwriter
George Nyasulu
Songwriter
Bill Chayamba
Songwriter
Brian Jonas
Songwriter
McPitrie Mpate
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Richard Billy
Producer
M.O.D Recording Studio
Producer
Chisomo Nkhoma
Producer
Lirik
Wati bwa?
Wati cha?
Wayimba phone nthawi yolakwika
Wati bwa?
Wati cha?
Wayimba phone nthawi yolakwika
Ndili pa Phokoso
Kuno nde kwayaka moto
Ndili pa Phokoso
Kuno nde kwayaka moto
Wati bwa?
Wati cha?
Wayimba phone nthawi yolakwika
Wati bwa?
Wati cha?
Wayimba phone nthawi yolakwika
Ndili pa Phokoso
Kuno nde kwayaka moto
Ndili pa Phokoso
Kuno nde kwayaka moto
Tiyankhulane Monday bwa
Ndidye kayetu zi money bwa
Nkanayankha, koma wachedwa
Phone yi izingolira ngati namfedwa
Tikakudula tioneke amwano
Chonsecho pa phone mmangokamba zinthano
Wayimba phone ukusokoneza phwando
Takuuza kale tili mkati ngati mwado
Ine ndine Baxxy aise (wati bwa?)
AKA sugar ntape aise (wati cha?)
Gin yu si Fanta aise (wati bwa?)
Real life si fantasy (wati cha?)
Iwe ndati ndine Baxxy aise (Baxxy aise)
Tikufaka zima punch aise (Punch aise)
Wafaka Nali mu Cactus eti? (Cactus eti)
Mukuchaser so Hunters eti? (Taonani, taonani, taonani)
Wati bwa?
Wati cha?
Wayimba phone nthawi yolakwika
Wati bwa?
Wati cha?
Wayimba phone nthawi yolakwika
Ndili pa Phokoso
Kuno nde kwayaka moto
Ndili pa Phokoso
Kuno nde kwayaka moto
Wati bwa?
Wati cha?
Wayimba phone nthawi yolakwika
Wati bwa?
Wati cha?
Wayimba phone nthawi yolakwika
Ndili pa Phokoso
Kuno nde kwayaka moto
Ndili pa Phokoso
Kuno nde kwayaka moto
Kulandira ma flowers zili mu DNA
Ndimafuna credit funsa a TNM
Koma ngati ndayipeza sindiyimba yimba
Ngati ndayimba, ndachemetsa stage ukundidziwa ine
Lero sober man saapeza, ntaji
Ma guy inu kodi mmacheza, bwanji?
Samwa mowa wangozizidwa, Sangie
Ine ndi merchah, merchant, Naji
Bee phone yake ikungoti krrr! krrr!
Ife sitimadalira crrr! crew!
Ana a fly, prrr! prrrr!
Ooneka super, grrr! glue
Iwe, zitheka bwanji kuyimba phone
Mmalo mondipatsa plan, undipatsa moni
Ati poti kunja kwacha basi hie, morning
Ndiyankha bwanji sukukamba za my money
Wati bwa?
Wati cha?
Wayimba phone nthawi yolakwika
Wati bwa?
Wati cha?
Wayimba phone nthawi yolakwika
Ndili pa Phokoso
Kuno nde kwayaka moto
Ndili pa Phokoso
Kuno nde kwayaka moto
Wati bwa?
Wati cha?
Wayimba phone nthawi yolakwika
Wati bwa?
Wati cha?
Wayimba phone nthawi yolakwika
Ndili pa Phokoso
Kuno nde kwayaka moto
Ndili pa Phokoso
Kuno nde kwayaka moto
Written by: Bill Chayamba, Brian Jonas, George Nyasulu, Happy Bakolo, McPitrie Mpate

