album cover
Choncho
73
Hip-Hop/Rap
Choncho was released on November 30, 2024 by Crispy Malawi as a part of the album Digital Maskini
album cover
Release DateNovember 30, 2024
LabelCrispy Malawi
LanguageEnglish
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM69

Credits

PERFORMING ARTISTS
Crispy Malawi
Crispy Malawi
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Chifundo Chingaipe
Chifundo Chingaipe
Composer
PRODUCTION & ENGINEERING
Farouk f9 Mitochi
Farouk f9 Mitochi
Mixing Engineer

Lyrics

Olo No make up ukuoneka bwino choncho
Umandiwaza Ukamaoneka Choncho
Umandiwaza uka dressa choncho
Unandikomzekera Choncho
Unapanga Ubale Wamadzi ndi Soap
Uyambe ku Fire ukubweza moto
International Siza Local
Digital Maskini Wavaya Global
Wandipasa phone number nzake ali pompp
Ndukuuza Sungagwire Ngati ulibe khodo
Akufila Fragrance,Freckled Mo nnda mixa ndi Torm Ford
Ngati ukufuna utha ku halla nimangomemya Phone call
What’s up with your T shirt?
Ulibe abale kapena KnQ
Ndaonela Skirt yonga’amba kuti palibe akuku soka
Ndi Mfana ozimva or akasiya ku Talka
Akakwiya amandi Blocker
Akamapita ndimamukoka
Olo No make up ukuoneka bwino choncho
Umandiwaza Ukamaoneka Choncho
Umandiwaza uka dressa choncho
Unandikomzekera Choncho
Unapanga Ubale Wamadzi ndi Soap
Uyambe ku Fire ukubweza moto
International Siza Local
Digital Maskini Wavaya Global
Choncho nde uziti sumandifila Choncho
Munthu umangofuna komwe ndiliko ukhale komko
Ndi nthawi yanga ona Nthawi ikuti spe o’clock
Siwe snack ndiwe full meal tipase mpeni ndi fork
Huh
Beef kudya Ndekha
Pa level nditadekha
Movie Tiku Major
Mix kamangoseka
Ex wake akulenga
Uli ndi mfana Otentha
Zinamupeta§zinamutembenuza
Anatumiza Leka
Olo No make up ukuoneka bwino choncho
Umandiwaza Ukamaoneka Choncho
Umandiwaza uka dressa choncho
Unandikomzekera Choncho
Unapanga Ubale Wamadzi ndi Soap
Uyambe ku Fire ukubweza moto
International Siza Local
Digital Maskini Wavaya Global
Written by: Chifundo Chingaipe
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...