Krediler
PERFORMING ARTISTS
Phyzix
Performer
Jae Cash
Performer
Charisma Madness
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Noel Phyzix Chikoleka
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
BFB
Producer
Şarkı sözleri
Very good, very good
It’s only entertainment
Yeah, Chariz
Jae Cash, Jae Mullah
How is it my life if I play by your rules?
If a **** mess up, I give ‘em the deuce
I work hard ine sindinena tchuzi
Pa hustle yanga sindikhalapo pa tchuthi
Inedi, inedi sindizafa mphawi
Uzikankha, uziphusha, siuzafa mphawi
Inedi, inedi sindizafa mphawi
Uzikankha, uziphusha, siuzafa mphawi
Not your regular rapper, Phyzix the Mountain Goat
Ndakhala ndikuswa zakazaka like you never thought
Mumuwuze mwini nyumba ndine mwini plot
Alimbana bwanji ndi mikunda iye ali toti?
I’m doing this rap thing, it’s a gift thing
Kundishosha ineyo ndi mbola like a bee sting (ehh)
I’m tryna get this money, ine ndi gang-gang
Timakankha ngini everyday it’s the same thing (eish)
Ndimalawilira daily ma hustle
Ndizaziwone ndili bho, ndisanatseke maso
Ndimafuna kuti tea ndizamweso
Mdala inapita, masteni anapitaso
I hope you understand things I do
Sine munthu wotengeka womangoti “me too” (njee)
I do what I do ‘cause I need to
Ndili ndi ma responsibility ngati munthu (very good)
How is it my life if I play by your rules?
If a **** mess up, I give ‘em the deuce
I work hard ine sindinena tchuzi
Pa hustle yanga sindikhalapo pa tchuthi
Inedi, inedi sindizafa mphawi
Uzikankha, uziphusha, siuzafa mphawi
Inedi, inedi sindizafa mphawi
Uzikankha, uziphusha, siuzafa mphawi
The only way in was to break the rules
We took the game over, don’t know if you heard the news
Kwathu tili na moto, you snooze you lose
Ndine mbuzi imadya ma rapper, not mawuzu
Nenzo ziba one day I’m gonna make it, for now lemme fake it
Mu DM bafana bali naked
Nyimbo zathu zi na message, ka ili ndiye essence
Kulibe achilamula ku patience
Take off my plate you probably never eat again
‘Cause you’ll be dead and gone, ****, til we meet again
I’m born ready, ni challenge if you need a game
Ndine FIFA ili chip, I’ve been in the game
They really tried to break us
Noziba kuti Jae Cash ndiye ali na potential yo crossa ko ma borders
Mpaka ma haters kukhala ma supporters
Nenze ba lunkumbwa pa ni trainela mu ma Jordan’s
How is it my life if I play by your rules?
If a **** mess up, I give ‘em the deuce
I work hard ine sindinena tchuzi
Pa hustle yanga sindikhalapo pa tchuthi
Inedi, inedi sindizafa mphawi
Uzikankha, uziphusha, siuzafa mphawi
Inedi, inedi sindizafa mphawi
Uzikankha, uziphusha, siuzafa mphawi
Sindizafa mphawi
Siuzafa mphawi
Written by: Noel Phyzix Chikoleka

