album cover
Chiperoni (Nyanja, 1959)
album cover
Chiperoni (Nyanja, 1959) was released on October 9, 1991 by RetroAfric as a part of the album Shalapo
AlbumShalapo
October 9, 1991
LabelRetroAfric
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

Mayi, mowa wa chiperoni mu plantaya
Mayi wakuti satu kwapele nditu, amayi
Mayi, mowa wa chiperoni mu plantaya
Mayi wakuti satu kwapele nditu, amayi
Ndlama sizinkala patumba mama
Banja pa nyumba kufa njala mama, chisoni
Ndlama sizinkala patumba mama
Banja pa nyumba kufa njala mama, chisoni
Mayi, mowa wa chiperoni mu plantaya
Mayi wakuti satu kwapele nditu, amayi
Mayi, mowa wa chiperoni mu plantaya
Mayi wakuti satu kwapele nditu, amayi
Chiperoni ndi mowa wabwino nditu
Ukala monga nichakulya nditu, amayi
Chiperoni ndi mowa wabwino nditu
Ukala monga nichakulya nditu, amayi
Mayi, mowa wa chiperoni mu plantaya
Mayi wakuti satu kwapele nditu, amayi
Mayi, mowa wa chiperoni mu plantaya
Mayi wakuti satu kwapele nditu, amayi
Ndlama sizinkala patumba mama
Banja pa nyumba kufa njala mama, chisoni
Ndlama sizinkala patumba mama
Banja pa nyumba kufa njala mama, chisoni
Mayi, mowa wa chiperoni mu plantaya
Mayi wakuti satu kwapele nditu, amayi
Mayi, mowa wa chiperoni mu plantaya
Mayi wakuti satu kwapele nditu, amayi
Written by: Alick Nkhata
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...