album cover
Agone Akome
194
Reggae
Agone Akome was released on October 29, 2012 by Malawi Goodlife as a part of the album Fifteen Fifteen
album cover
Release DateOctober 29, 2012
LabelMalawi Goodlife
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM160

Music Video

Music Video

Credits

PERFORMING ARTISTS
Lucius Banda
Lucius Banda
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Lucius Banda
Lucius Banda
Composer

Lyrics

Oooh whoo
Ooh whoa, oh yeah
Ooh, ay yah-yah-yah yoh
Buyaka
Lero wakoma poti wamwalira
Adakali moyo mumkamutcha galu
Dzina lake mukumutchula mfumu
Ankasowa madzi pamene amkadwala
Lero wamwalira mwapanga phwando
Mukumadya nyama yomwe amkasilira
Ampingo mukuyimba nyimbo mokweza
Munali kuti dzana amkasowa pemphero
Musamadikire agone
Ndiye mudzikamba zabwino
Chovuta ndi chani abale?
Kumuyamika akali moyo
Ngakhale adani anuwo
Ali ndi pena pokomera
Ndi diso lanji mulinalo?
Limangoonatu zoyipa
Mwana wantchitoyu mwakhala naye
Nthawi yayitali wakulemeletsani
Muli ndi zigayo, ma lodge ma farm
Ma shop ndima lory mwapanga ndi Iye
Chovuta ndi chani kumupatsa ka phapha
Adzipanga matola, adzakudalitsani
Koma ndadziwa galimoto mudzampatse
Lidzakhala bokosi akadzamwalira
Musamadikire agone
Ndiye mudzikamba zabwino
Chovuta ndi chani abale?
Kumuyamika akali moyo
Ngakhale adani anuwo
Ali ndi pena pokomera
Ndi diso lanji mulinalo?
Limangoonatu zoyipa
Woyimba ambiri ngakhale azisudzo
Akulowa ndale chifukwa ndi chani?
Chifukwa inuyo m'malo mowa supporter
Mumakonda akunja iwowa kuwasiya
Makabani atha kuyimba wakunja
Ten million amangompatsa
Ine wakuno 50 thousand mumanenelera kumati ndadulitsa
Musamadikire agone
Ndiye mudzikamba zabwino
Chovuta ndi chani abale?
Kumuyamika akali moyo
Ngakhale adani anuwo
Ali ndi pena pokomera
Ndi diso lanji mulinalo?
Limangoonatu zoyipa
Musamadikire agone
Ndiye mudzikamba zabwino
Chovuta ndi chani abale?
Kumuyamika akali moyo
Ngakhale adani anuwo
Ali ndi pena pokomera
Ndi diso lanji mulinalo?
Limangoonatu zoyipa
Musamadikire agone
Ndiye mudzikamba zabwino
Chovuta ndi chani abale?
(Kumuyamika akali moyo)
(Ngakhale adani anuwo)
(Ali ndi pena pokomera)
Written by: Lucius Banda
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...