album cover
Misozi
141
Afro-Beat
Misozi was released on March 18, 2022 by Wakisa James Music as a part of the album Misozi - Single
album cover
Release DateMarch 18, 2022
LabelWakisa James Music
LanguageEnglish
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM51

Music Video

Music Video

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Wakisa Chiwona
Wakisa Chiwona
Songwriter

Lyrics

Zizatheka Lit
Zizayenda Lit
Langa ndi funso
Zaka zupita nthawi yupita Yehova ndikumbukireni
Za anzanga zinatheka zanga zaima ndikonzereni
Banja ndi malifuna koma za amuna ndimangokhumudwapo
Amango ndi user ndikundilumitsa chakudanso
Is this how it's going to be Moyo wowawa kukhala lonely
I need somebody to hold me down when am falling
They kept on saying beib hold/am beautiful
I will smile in the scarsIt's going to be alright and it won't be long
Koma vuto ndukula Zaka 34 no mwamuna
Mesa ndife Maluwa Naneso mwana ndimamufuna
Moto Moto Moto I feel like ndi giveee
Pa anthu onsewa zoona Nkazi opanda mwana n'kakhale ine
Ili ndi dziko lokenderaAaah I think ndine olodzedwa
Nde zimandikhuzaaa
Misozi
Ndili pa Moto Moto MotoI feel like ndi giveee
Pa anthu onsewa zoona Mai okanika n'kakhale ine
Ili ndi dziko lokenderaAaah I think ndine olodzedwa
Nde zimandikhuzaaa
Misozi
Mesa mphatso ya mwanaMesa mphatso ya mwana ndi dalitso
Mesa ena amamusakaKoma ndi ine sizusiyana
Ndili ndi ana awiri wa muna ndi wa mkazi
Amangochoka koma pobwera ukoko ndi nkhani
Uchembere wanga ngat Mai ubale izi zoona
Nanga nditani ine ana asinthe sindigona
Nkachoka atazawasunge ndani tsogola sindiliona
Modzi yekha akanaphunzira nkanati bola
Ndungokhalira milanduMapokoso pokoso ndi mihau
Mwina nabeleka changuAna angawa ndilibe nao mau
Moto Moto Moto I feel like ndi giveee
Pa anthu onsewa zoona Nkazi opanda mwana n'kakhale ine
Ili ndi dziko lokenderaAaah I think ndine olodzedwa
Nde zimandikhuzaaa
Misozi
Ndili pa Moto Moto MotoI feel like ndi giveee
Pa anthu onsewa zoona Mai okanika n'kakhale ine
Ili ndi dziko lokenderaAaah I think ndine olodzedwa
Nde zimandikhuzaaa
Misozi
Zizayenda Liti Tsiku liti
Zizatheka Liti
Tsiku liti Misozi
Ine misozi
Wakisa misozi
Written by: Wakisa Chiwona
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...