歌词

Alick Macheso, agitate of Sungura, atomic bomba
Abambo anga inu, zomwe munapanga sizinthu zabwino ndithu
Abambo anga inu, zomwe munapanga sizinthu zabwino ndithu
Ndizabwino kwainuyo, koma kwaine sizomwe, chimodzimodzi ndi amayii
Ndizabwino kwainuyo, koma kwaine sizomwe, chimodzimodzi ndi amayii wanga oooo
Kunditayirira ine ngati mbuzi ine, abambo anga mulibe chisoni
Kunditaya, Kunditaya, kunditayira mudzenje abambo anga ine ndithu
Kunditaya, Kunditaya, kunditayira muchitini abambo anga ine ndithu
Kunditayirira ine ngati mbuzi ine, abambo anga mulibe chisoni
Munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
Munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
Munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
Munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
Abambo anga ine (Abambo anga ine), umoyo wanga ine (umoyo wanga ine), wokulira muumphawi (wokulira muumphawi), ndine mwana wa masiye ine (ndine mwana wa masiye ine)
Zomvetsa Chisoni, ndithu siumoyo wosangalatsaa
Ndilibe chomwe ndingapange ineyo chifukwa ndine mwana
Chimene chinakupatsani kuti mupange zimenezi
(Abambo anga inee ndithu)
Ndilibe chomwe ndingapange ineyo chifukwa ndine mwana
Chimene chinakupatsani kuti mupange zimenezi
Written by: Alick Macheso
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...