album cover
Loyalty
album cover
Skladba Loyalty vyšla 12. srpna 2023 VAN NGONGO ENTERTAINMENT na albu Mzaliwa
AlbumMzaliwa
12. srpna 2023
ŠtítekVAN NGONGO ENTERTAINMENT
JazykEnglish
BPM84
Melodičnost
Akustičnost
Valence
Tanečnost
Energie

Texty

Yeah yeah yeah (Nyanda made it)
Yeah
Anamugulira benz
Pa birthday akaziyendela
Anampezela vephi
Sanalore mwanakazi azivutika
Koma ukamatha mwezi
Siyimalowa mwanakazi achite recharge
Mumamuyika dp mwezi onse osamusintha (yeah eh)
Koma akati adze malawulo umakuwotcha ndiwe dzulo
Anzako akakuyimbira wezulo
Unkayesa ngati ndi bodza
Akunama yeah eh-eh
Utha kumukonda monse momwe ungafune
Utha kumupatsa zonse zomwe angafune eh-eh
Koma adziwe loyalty is a choice
Loyalty is a choice, loyalty is a choice
Eya loyalty is a choice
Loyalty is a choice, loyalty is a choice yeah
Si material things
Chikondi chilibe fees
Ngati samakukonda sangakhale
Olo utamumangira mpanda
Uzamupeza ali panja
Wekhaso mkuzadabwa
Kani zimatere?
Koma akati adze malawulo umakuwotcha ndiwe dzulo
Anzako akakuyimbira wezulo
Iih yeah yeah
Utha kumukonda monse momwe ungafune
Utha kumupatsa zonse zomwe angafune eh-eh
Koma adziwe loyalty is a choice
Loyalty is a choice, loyalty is a choice
Eya loyalty is a choice
Loyalty is a choice, loyalty is a choice yeah
Sungamulipire kuti akhulupilike
Ngati amafuna, amafuna
Amafuna, amafuna adzaonetsa
Izi zoti n'namugulira (galimoto)
Izi zoti n'nnamuchitira (chilichonse)
And you expect loyalty in return
Udzalira, udzalira yeah!
Utha kumukonda monse momwe ungafune
Utha kumupatsa zonse zomwe angafune eh-eh
Koma adziwe loyalty is a choice
Loyalty is a choice, loyalty is a choice
Eya loyalty is a choice
Loyalty is a choice, loyalty is a choice yeah
Utha kumukonda monse momwe ungafune
Utha kumupatsa zonse zomwe angafune eh-eh
Koma adziwe loyalty is a choice
Loyalty is a choice, loyalty is a choice
Eya loyalty is a choice
Loyalty is a choice, loyalty is a choice yeah
Written by: Shafie Phiri
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...