Kredity

PERFORMING ARTISTS
Dirty flo
Dirty flo
Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Prince John Mtaya
Prince John Mtaya
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
F9ine
F9ine
Engineer

Texty

Ati Iye Ndi F-F Nine
Oh King Geoffy haha
Yeah Dirty yea, yea
Yanga Ndi yomweyi, I'm okay
Ndikangofika kuchoka aliyense anabwera
Dirty anabwera
Dirty anabwera
Yeah
(Tamatiye)
Hi , wandipeza ndili high pa roof (High pa roof)
Mfana wokwiya koma sindinakwiyile munthu
Pakatipa nafinyika koma mbali, mbali munalibe munthu
I don't like to dance ndimangomilizitsa ma move
Huh, Ndinakonda kuyisiya life iyi
Koma nanga nchite bwanji Ndi drive iyi
Runner Ngini ndima dogs ngati afika pa ugalu
I've been the served kusunga ma change
Olo utati usunge nthawi sungandipeze
Boys yake yozizira backdoor sinatseke
Mitu yake yopepuka kupeza bag singahede
Baby girl watengeka nane ndisanamutenge
Ndamuuza ukhole ma friends tikhale ma friends
Samandipange text, Samandipange vex
Gangster wapa TikTok sungandichallenge
Hi, wandipeza ndili high pa roof (High pa roof)
Mfana wokwiya koma sindinakwiyile munthu
Pakatipa nafinyika koma mbali, mbali munalibe munthu
I don't like to dance ndimangomilizitsa ma move
Huh, Ndinakonda kuyisiya life iyi
Koma nanga nchite bwanji Ndi drive iyi
Runner Ngini ndima dogs ngati afika pa ugalu
Written by: Prince John Mtaya
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...