album cover
Mabala
album cover
Mabala wurde am 10. März 2023 von Alltone Music als Teil des Albums Mabala - EP veröffentlicht
Released10. März 2023
LabelAlltone Music
SpracheEnglish
BPM95
Melodizität
Akustizität
Valence
Tanzbarkeit
Energie

Musikvideo

Musikvideo

Songtexte

Oooh
Pena mtima umawawa (mtima umawawa, mtima umawawa)
Achuluka ndi mabala (ndi mabala, mabala)
Pena mtima umawawa (mtima umawawa, mtima umawawa)
Achuluka ndi mabala (ndi mabala, ndi mabala) no, ey
Osanama ndikukhala movutika, ngakhale ndimalimbika
Loto mkukhala lopita Jamaica
Poti njira ya Jamaica
Koma ngakhale ndipushe ndilimbikire bwa
Kungochuluka ndi kupondelezedwa
Kukhomeleledwa komanso kuphweketsedwa
Eti olo nkome bwanji singapose thobwa
Amayine, Malawi ndisimba bwanji mtendere mu umphawi
Potitu zonsetu ndi nthawi
Mkumbuka mawu ananena mayi
Pena mtima umawawa (umawawa mtima)
Achuluka ndi mabala (achuluka mabala)
Pena mtima umawawa (umawawa, mtima)
Achuluka ndi mabala (Achuluka luka mabala)
Mabala, mabala, mabala
Mabala, mabala, ey
Mchere wa muthukuta ndi misonzi yanga (mmh)
Ndiye mankhwala amabala anga (anga)
Ambiri simusamala za mavuto anga (mmh)
Jehovah yekha ndiye ngaka yanga (yanga yeah)
Kuchokera pobadwa, n'nadziwa kulira nsanadziwe kuseka
M'mene ndimkakula, n'nadziwa magobo nsanadziwe kusewela
Mtima umawawa, umawawa mtima
Achuluka ndi mabala, achuluka ndi mabala
Pena mtima umawawa, umawawa mtima
Achuluka ndi mabala, achulula luka mabala
Ndukukuwuzani misozi yanga itha kukumizani
Litha kukukulani thukuta lomwe ndakhetsa mu mtima
Umawawa, umawawa mtima
Achuluka ndi mabala, achuluka ndi mabala
Pena mtima umawawa, umawawa mtima
Achuluka ndi mabala, achulula luka mabala
Umawawa mtima
Achulula mabala
Umawawa mtima
Achuluka luka mabala
Written by: Chiccondi Mungwa
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...