Songtexte

Nthawi yakwana wokondedwa Yowonetsa chi khristu Munthu oyipa musamubwezere choipa Kuti aphunzire zachikondi Anali kunyoza makolo ako Palibe kanthu ndizambuyo Maso patsogolo mothokoza Chauta Watichitira zazikulu Musaweruze amzanu Kuwopa mkwiyo wa Atate Mulungu amawona zonse zochita wanthu Azadziwa mwini wake Ntchito yathu masiku ano Tikulitse chimvano Amayi athu tonse ndi m'modzi Malawi Tikondane wina ndi mzake Anatisambula tikabwezere Maganizo achikunja Musamulore inu satana atenge mitima yanu Mudzasanduka akapolo Atsogoleri athu ndi a mtendere Ndife odala Malawi Palibe kabwino kochokera mu kumenyana Chizangokula chisoni Anthu oyenda mumdima Anawona kuwala Yesu ndiye njira chowona ndiponso moyo Tidzafika kuchilonjezo Tipemphere molimba Tithokoze Ambuye Atisungebe moyo ndikutigawira nzeru Tiyende mu kuwala kwake Chikondi ndicholeza mtima Chikondi chilibe nkhanza Chikondi sichidzitama Chikondi chilibe kaduka Chikondi chilibe malire Sitikondwa pasowa chilungamo Chikondi chimapilira Sichilankhula zolakwa za wena Chikondi ndicholeza mtima Chikondi chilibe nkhanza Chikondi sichidzitama Chikondi chilibe kaduka Chikondi chilibe malire Sitikondwa pasowa chilungamo Chikondi chimapilira Sichilankhula zolakwa za wena Chikondi ndicholeza mtima Chikondi chilibe nkhanza Chikondi sichidzitama Chikondi chilibe kaduka
Writer(s): Sir Paul Banda Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out