album cover
Mtima
album cover
Mtima fue lanzado el 3 de marzo de 2025 por Broken Crayons como parte del álbum To The Moon & Back
3 de marzo de 2025
Sello discográficoBroken Crayons
IdiomaEnglish
BPM99
Melodía
Nivel de sonidos acústicos
Valence
Capacidad para bailar
Energía

Video musical

Video musical

Letra

Ndimafuna utapeza Chikondi
Utagwa Chikondi
Tidzaone ma post
Ma heart emoji
Anzako kusilira
Mene love uyifilira
Zizafike pokoma
Zikafikapo
Ndikufuna Azakuswe mtima
Azakuswe mtima
Udzaone mdima iwe
Azakuswe mtima
Azakuswe mtima
Azakuswe mtima
Uzadziwe karma iwe
Udzaone mdima
Opusa ndine pokukonda mmmhu
Ndinalakwa kukukonda?
When I gave you all of me all my heart butterflies kumati mwala ndaponda
Koma palibe zobwelera ndinasaignila
Uzangofila mene ine ndinafilira
Mtima wanga sipadziko - ungopitilira
Wafika joker ameneyo angokufeelaaaa
Nde tachiyese Chikondi ungochipatsa chance
Uzafuna zambiri azakupatsa less
Ma sabaweli ine ndi kudikila mess
As if I do care I'll say God bless
Koma pansi pamtima ndizadikila karma izakupeze ndikapeza wina
Koma pansi pa mtima ndinaipatsa karma map akwanu singapite kwina
Ndimafuna utapeza chikondi
Utagwa chikondi
Tidzaone ma post
Ma heart emoji
Anzako kusilira
Mene love uyifilira
Zizafike pokoma
Zikafikapo
Ndikufuna adzakuswe mtima
Adzakuswe mtima
Udzaone mdima iwe
Adzakuswe mtima
Adzakuswe mtima
Adzakuswe mtima
Uzadziwe karma iwe
Udzaone mdima
Ndipo adzakwatile wina
Iwe uzanyuke mtima
Uzaone mdima
Pansi pa mtima ndinaipatsa karma map akwanu singapite kwina
Ndimafuna utapeza chikondi
Utagwa chikondi
Tidzaone ma post
Ma heart emoji
Anzako kusilira
Mene love uyifilira
Zizafike pokoma
Zikafikapo
Ndikufuna adzakuswe mtima
Adzakuswe mtima
Udzaone mdima iwe
Adzakuswe mtima
Adzakuswe mtima
Adzakuswe mtima
Uzadziwe karma iwe
Udzaone mdima
Written by: Daniel Kasinjeni, Praise Umali
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...