album cover
album cover
Ofewa fue lanzado el 3 de julio de 2026 por Hit Factory Records, Exclusively Distributed Under Trappybeats. & Hope Cizzle. (Pty) Ltd como parte del álbum Internet Famous - EP
3 de julio de 2026
Sello discográficoHit Factory Records, Exclusively Distributed Under Trappybeats. & Hope Cizzle. (Pty) Ltd
IdiomaEnglish
BPM113
Melodía
Nivel de sonidos acústicos
Valence
Capacidad para bailar
Energía

Video musical

Video musical

Letra

Ngongole mpakana kutenga ngongole
Kutenga katapila cholinga muuchape
Friday musangalale
Nzakoyo ali pa will
Iwe Busy ku sorter ma bill
Akwawo onse alipa masm
Inu kwanu mukungodyera mpiru
Nde chaser money osati ma honeys
Umasaukisa moyo wama party
Olo tiphule mochedwa titelekabe
Ngati usali Nepo Baby
Osapanga chibwana iwe
Mafana Ofewa
Osawa Tengera
Akupweteka
Akuvulaza Mthumba
Mafana Ofewa
Osawa Tengera
Akupweteka
Akuvulaza Mthumba
Mafana Ofewa ofewa
Mafana Ofewa ofewa
Mafana Ofewa ofewa
Mafana Ofewa ofewa
Pa bill yanga madzi akutanipo
Zovala ndimavala za shop
Ku drippa nde ndi non stop
Ku drippa kukhala ngati nyanja
Nde vuto nane ndikasanja
Ndimafuna kuti ndigone panja
Ndangozindikira zatha zathapo
Ku stantila ma galimoto akwawo
Ma house party munyumba yakwawo
Yalakwa Yalakwa
Mnthumba mwanga ndasala ndi 2 kwacha
Osasonkha lero sakuudina nawo
Osasonkha lero sakuudina nawo
Mafana Ofewa
Osawa Tengera
Akupweteka
Akuvulaza Mthumba
Mafana Ofewa
Osawa Tengera
Akupweteka
Akuvulaza Mthumba
Mafana Ofewa ofewa
Mafana Ofewa ofewa
Mafana Ofewa ofewa
Mafana Ofewa ofewa
Written by: Hope Cizzle Ngalande, Ian Trappybeats Ngalande
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...