Clip vidéo
Clip vidéo
Crédits
INTERPRÉTATION
Patience Namadingo
Interprète
COMPOSITION ET PAROLES
Namadingo
Paroles/Composition
PRODUCTION ET INGÉNIERIE
Moshu
Production
Soundbwoy
Ingénierie de mixage
Paroles
Uvomereze mbali yako wachita
Kodi uchite kudzichekacheka
Kut amvetsetse usachite kumuumiliza kut mukondane
Kodi udzimupembedza kut akukonde usachite kuyaluka nazo
Chikondi sakaka kakamizana
Chikondi sitikakamila
Chikondi sakaka kakamizana
Chikondi sitikakamila
Ngati watopa mulekele
Mulekele, iii mulekele
Ngati walema muchokere
Muchokere, iii muchokere
Osakakamizana
Abwere ndi nzeru zake
The mind, the body, the soul
Adzikukonda iwe udzidziwaso
Udzichita kumva kut wina palibeso
Zija zomalotana mukatseka maso
She be the queen nah iwe the king in a castle
Not vija zombetsana kuwawaso
Chikondi sakaka kakamizana
Chikondi sakaka kakamizana
Chikondi sitikakamila
Chikondi sitikakamila
Ngati watopa mulekele
Mulekele, iii mulekele
Ngati walema muchokere
Muchokere, iii muchokere
Ngati watopa mulekele
Mulekele, iii mulekele
Ngati walema muchokere
Muchokere, iii muchokere
Osakakamizana
Chikondi sakaka kakamizana
Chikondi sitikakamila
Chikondi sakaka
Chikondi sakaka
Sakaka
Namadingo
Written by: Patience Namadingo