album cover
Addicted
album cover
Addicted est sorti le 27 mars 2023 par Independent dans le cadre de l'album Tomorrow
Date de sortie27 mars 2023
LabelIndependent
BPM
Qualité mélodique
Acoustique
Valence
Dansabilité
Énergie

Paroles

Jay Emm
Mtima umangoti phaphapha
Mtima umangoti
Dru..Dru..Dru..Drumz
Ukangoti wachoka wee
Wachoka wee
Ukangoti wasuntha wee
Wasuntha wee
Mtima umangoti phaphapha Aah
Mtima umangoti phaphapha Aaaah
Coz I am addicted to you
It's not kuti iweyo mmakukaikira
Koma kungoti ineyo nnazolowela
Kukhala nawe Ah kukhala nawe
Sinfuna uzitalikila
Koma wina akangoti wakutenga
Ndzamulodza I swear
Ndzamulodza I swear
Ndzamulodza
Ukangoti wachoka wee
Wachoka wee
Ukangoti wasuntha wee
Wasuntha wee
Mtima umangoti phaphapha Aaah
Mtima umangoti phaphapha Aaaah
Coz I am addicted to you
I am addicted to you
I am addicted to you
Ayeee....Ayeee....Ayeee....Ayeee....Ayeee
Pena ndimangoti Unandidyetsa mankhwala
Kulikonse ndingapite ukuganizira
Ngati ndiwe mowa ayi singakusiye
Ngati ndiwe chamba ayi undipengetsa
Koma utangoti lero chatha
Aah singalore ine Aah singalore ine
Ndati singalore
Ukangoti wachoka wee
Wachoka wee
Ukangoti wasuntha wee
Wasuntha wee
Mtima umangoti phaphapha Aaah
Mtima umangoti phaphapha Aaaaah
Coz I am addicted to you
I am addicted to you
I am addicted to you
Ayeee....Ayeee....Ayeee....Ayeee....Ayeee
Dru....Dru....Dru...
Ukangoti wachoka wee
Wachoka wee
Ukangoti wasuntha wee
Wasuntha wee
Mtima umangoti phaphapha Aaaah
Mtima umangoti phaphapha Aaaah
Coz I am addicted to you
I am addicted to you
I am addicted to you
Ayeee....Ayeee....Ayeee....Ayeee....Ayeee

Loading...