Crédits
COMPOSITION ET PAROLES
Tadala Nkhundah Hollah
Paroles/Composition
Sidney Sagonjah Zulu
Paroles/Composition
PRODUCTION ET INGÉNIERIE
Justus
Production
TchuxTipatsePlan
Production
Nëfter
Production
Paroles
One spliff a day keep the evil away
One spliff a day keep the evil away
One spliff a day keep the evil away
One spliff a day keep the evil away
One spliff a day keep the evil away
One spliff a day keep the evil away
One spliff a day keep the evil away
One spliff a day keep the evil away
Yo check it
Yolimidwa pa Nyasa, uh
Golide weniweni no mizaza, uh
Mutu ukapweteka ndikuyasa
Pepa neighbor ngati zimakunyasa, uh
Inditenge,zindisiye ndili duuu kucheteka
Pena kuseka ngati mtima suu kupweteka
Mankhwala
Kuzitemela mumabala ndikakhala
Ndayenela kudwala ndikasala
Mitengo kuokela ngati m'malambe
Iyi ndizadya mpaka ndizakalambe
Ubwino wake kwa inu sarngakambe
A police ndi abale sangalande
Kwani
Imeneyo mma newspaper nde nkhani
Ku mtundako akuba koma lekani
Anangozazana anamaselempwani
How do you even tell this to a lame man?
Eh ndikuyasa
Moto,sindikuzima toto,kwanilitsa maloto
Kwathu ndikunyasa
Opeleka misonkho,onse olima mogo,angotsala ndi khokho
Zinthu zanyasa
Taona katangale, mzimu wa Matafale, lira mayi wawaye
Iwe dzuka nyasa
Zitsotso zitsatse,pa msika zitsatse,tsamba lobiliwira liyase
Written by: Sidney Sagonjah Zulu, Tadala Nkhundah Hollah

