क्रेडिट्स
COMPOSITION & LYRICS
Cuthbert Joya
Songwriter
Josephy Paul Alufandika
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Cuff-B Jimz
Producer
गाने
Uvomeleze zoti Ena sakukonda
Ena amakukonda
Kwa ena ndiwe kape
Kwa ena ndiwe dolo
Ena samagona nawe Tulo
Kumangofuna kumva zaiwe
Ena akukoona amanyasidwa nawe
But don't kill yourself ngati sakukonda
Don't kill yourself
Ngati ena sakuonda iwe
Ayoyoyoooo si iwe SUGAR
Ayoyoyo sungakomele aliyese
Ayoyoyooo Si ine sugar
Ayoyoyoyoo singakomere aliyese
Sindingakomere aliyense chi squad chigulu
Mulu umandikonda ondidaso ndi mulu
Kundiona ndikufooka amamenya nthungululu
Koma stulu ndi sitilu siingafike pa thebulo
Pomwe mukusunga mithulu,ndikukwera pachulu
Kuphusha-Suntha ndikuponda yanga ndiyamimbulu
Mungochedwa kundiwerenga siine mchere wamibulu
Ndikumvetsani ululu ngati sound ya ndulu
Nde mukamadoja mbuye amandiika pa-easy
Amandiuza palibe angasaize
Keep holding on yeh am holding on
Siine sugar chonde musamandijaile
Ayoyoyoooo si iwe SUGAR
Ayoyoyo sungakomele aliyese
Ayoyoyooo Si ine sugar
Ayoyoyoyoo singakomere aliyese
Umvetsetse izizi osawawidwa Mtima
Anthu Ena ndi akadzidzi nzeru zamu Mdima
Olo gulu likufire Iwo amaphweketsa
Usakakamire ataye akuchedwetsa
Do ya thing Do Ya thing
(Wah wah)
Just walk on your road
Do ya thing Do ya thing Do ya thing
Don't punish yaself do what you can afford
Usamafinyike Usamazunzike
Usabalalike Usazunguzike
Akakuonjeza Basi uwatsike
Anthu Ena ndi osatheka sangakuyamike
Ayoyoyoooo si iwe SUGAR
Ayoyoyo sungakomele aliyese
Ayoyoyooo Si ine sugar
Ayoyoyoyoo singakomere aliyese
Ayoyoyoooo si iwe SUGAR
Ayoyoyo sungakomele aliyese
Ayoyoyooo Si ine sugar
Ayoyoyoyoo singakomere aliyese
Written by: Cuthbert Joya, Josephy Paul Alufandika

