गाने

Aseh Trappy! Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa) Miseche Ndizi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!) Ndalama Ndalama (Aah aah ah) Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa) Miseche Ndizi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!) Ndalama Ndalama (Aah aah ah) Mpaka akudana nane akuyesa ndili ndi ndalama Man muzingo hasser hasser basi Nkhani nde ndikungoyika calm Mene ndikuspendela sindingakuwuze Mene tukazisaka sindinakuwuze Ngati ulibe sungandiuze Ndi kale ndinadandaula kuti life ikuyenda Slow-Mo Ine ayi ndili mkati momo Because I be spending like Jomo Ndalama ndi nsamo Olo andinyoze, andikambe, andiseke ine vibe ndi hundrede Olo andihate ine chete ma plan agona pa mandede Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa) Miseche Ndizi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!) Ndalama Ndalama (Aah aah ah) Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ma plan) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa) Miseche Ndizi Nkhani (Ayo Trappy!, Tiyeni!) (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!) Ndalama Ndalama (Tiyeni!, Tiyen!,Tiyeni! eish!) Ndalama Ndalama (Aah aah ah) Zibwana ndimapanga (Zibwana ndimapanga) Posaka ndalama (Posaka ndalama) Zibwana sitipanga (Zibwana Sitipanga) Posaka ndalama (Posaka ndalama) Ndiye ndiwe ndani? umatani? Usandipatse busy Dzina ndani? umatani? Usandipatse busy Ndiwe ndani? umatani? Usandipatse busy Dzina ndani? umatani? Usatipatse busy Eish! Maluzi Maluzi Maluzi Maluzi Maluzi Maluzi (Musiye Mzako) Maluzi Maluzi Maluzi Maluzi Maluzi Maluzi (ooh Musiye Mzako) (M'siye Nzako) Maluzi Maluzi Maluzi Maluzi Maluzi Maluzi (Musiye Mzako) (Eish!!) M'siye Nzako Maluzi Maluzi Maluzi Maluzi Maluzi Maluzi M'siye Nzako Ndakuthela Ma Plan (Maluzi Maluzi Maluzi) (Maluzi Maluzi Maluzi) Kodi Nnalakwa Chani (Maluzi Maluzi Maluzi) (Maluzi Maluzi Maluzi) (M'siye Nzako) Ndakuthela Ma Plan (Maluzi Maluzi Maluzi) (Maluzi Maluzi Maluzi) Kodi Nnalakwa Chani (Maluzi Maluzi Maluzi) (Maluzi Maluzi Maluzi) (M'siye Nzako) Ndalama Ndalama Maluzi Maluzi Maluzi M'siye Nzako Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa) Miseche Ndizi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!) Ndalama Ndalama (Aah aah ah) Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa) Miseche Ndizi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!) Ndalama Ndalama (Aah aah ah)
Writer(s): Ian Derrick Ngalande Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out