क्रेडिट्स
COMPOSITION & LYRICS
Teddy Makadi
Songwriter
Tawanda Mpando
Songwriter
Daisy Mpando
Songwriter
Hope Ngalande
Songwriter
गाने
Lost My Forever - Twnda x Teddy MakadiHook
Oh ndimachedwelanji ine
Ka'ndimatengelanji nthawi
Ngati nthawi ndi mzanga
Now you are gone
In anothers arms
I've lost my forever
Oh I've lost my forever
Oh I've lost my forever
I've fumbled the bag
Ndabudula ndiwo
I've lost my forever
Teddy
I took too much time sindinakuuze zonse
Zakukhosi kwanga usananditsomphoke
N'nanyalaza iwe usanawoloke
M'manja mwachidodo mwayi sindinawutole
If I knew, that tsiku lina nzasimba za you
Baby mwina ndikanapusha for you
N'nawelengela girl I thought you knew
Hook - Twnda
Oh ndimachedwelanji ine
Ka'ndimatengelanji nthawi
Ngati nthawi ndi mzanga
Now you are gone
In anothers arms
I've lost my forever
Oh I've lost my forever
Oh I've lost my forever
I've fumbled the bag
Ndabudula ndiwo
Outro - Twnda
This is the story
The pitiful story
Of how pride and ego
And kusatheka
Lost me forever
Mpange bwanji kuti abwelele
Bwelele Bwelele Bwelele Bwelele Bwele
Bwelele Bwelele Bwelele Bwelele Bwele
Mwina ndikhwimire kuti iyeyo
Iyeyo abwelele
Mpange bwanji kuti abwelele
Bwelele Bwelele Bwelele Bwelele Bwele
Bwelele Bwelele Bwelele Bwelele Bwele
Mwinandipemphere kuti iyeyo
Iyeyo abwelele
Written by: Daisy Mpando, Hope Ngalande, Tawanda Mpando, Teddy Makadi