क्रेडिट्स

PERFORMING ARTISTS
Dirty flo
Dirty flo
Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Prince John Mtaya
Prince John Mtaya
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Timo Beatz
Timo Beatz
Producer

गाने

Ati Iyeyo Ndi F-F nine
Yeah Dirty yeah
Nde ndinakumana ndika baddie kenakake
Nde nangokawonetsa Naneso Ndi bad news
(Timothy Got The Fire Beats no matter what it is)
Wagwan, Wagwan Chinachake
Yeah content yoti, dikila umve mene inayendela eti
Anthu awiri sangayende, asanapangane
Real recognize real yeah, deal inapita kwa deal
Kanzake kofatsa komabe sitikudziwa zomwe kumbali amakamvana
Innocent looks koma samaphana ndi ana
Kuthoka mophweketsa ati "uzapakula ukakula"
Ati ndi woyendayenda ndati "Naneso ndili pa tour"
Uh uh ukuyankhulitsa Ndi vumbuluke ndingoying'alula
Ine ndi yolakwa kale nthawi yochongetsa ndizibanduka
Ngati yalakwa pa den ine sikumalakwa pa den
Ngati ukupanga za geli part time ndi plenty
Nditha kupatsa test tiye tidyere limodzi
Chifukwa tikufana taste tonse yolakwa
Yolakwa, yolakwa imayenda yolakwa
Yolakwa, yolakwa yatengana yolakwa
Yolakwa, yolakwa imayenda yolakwa
Ndikadolo choncho tikuyilakwitsa titavala ma Nike sneakers
Kuzifila kudziwa she like "I know you ****"
I'm like "I know you sisters"
Atha kulowa onse azinzakowo
Ino ndimayilakwitsa sidzadza
Amawona ngati akumwa wine
Nda mixer zi shooter Ndi two spitter basi
Haha
Timothy Got The Fire Beats no matter what it is
Oh zinthu zakezo Ndi zotere
Written by: Prince John Mtaya
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...