Dari

PERFORMING ARTISTS
Mic Mash
Mic Mash
Vocals
Nathaniel Chaluchalu
Nathaniel Chaluchalu
Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Nathaniel Chaluchalu
Nathaniel Chaluchalu
Songwriter
Chisomo Phiri
Chisomo Phiri
Songwriter
Daniel Tadala Kasinjeni
Daniel Tadala Kasinjeni
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
M.anifest
M.anifest
Producer

Lirik

You see the problem is you say I don't listen
But you're not listening
You're not listen to me right now
You're not…. This is the thing you wanna talk first and then…
It's like ndukukakamiza everything ndukukajamiza
What do you mean ndukukakamiza
I've been forcing this thing from the get go
What are you talking about
You don't communicate
You don't communicate
Tungokhalira kuyambana
Lero wakwiya mawa ndakwiya komatu ife si ana Nde bwanji tingosiyana
Sikuti I don't care - ndimvetse
watopa nayo affair - ithetse
Koma fupa lokakamiza imatha kuswa mphika
Ndizotheka wachikondi wako uja kukutsika
Para vinthu va sugza
Para watondeka
Kapena watopa
Ndufuna undidziwitse
Para vinthu va sugza
Pala mwatondeka
Kapena mwatopa
Ndibwino undidziwitse ine
Ndidziwetse
Don't just go around corners
Don't make all this about you
Tayesa zosathekaaaa
Ndisiyeee ndipiteee
Ndidziwetse
Don't just go around corners
Don't make all this about you
Tayesa zosathekaaaa
Ndisiyeee ndipiteno
Aaaaaaaaa ndisiyeee ndipite
Eeeeeee set me freee
Aaaaaaaa ndisiyaaa ndipiteeeno
Eeeeeeee set me free
Look
The last time i checked comparison was a killer of Joy
If you wanna play games you buy a toy
Chikondi chanji
Chomafananiza ndi neighbor
Ati eeeh mmmhu chanthu chosabeba
Amuna ake anzanga amugulira iPhone iweyo undigulira yanga liti?
Best friend Panopa wavaya ku vacation ifeyo kodi tipitako?
Nditha kumazikonda ndekha
Moyo opanda iwe kumatheka
Nthawi ndichuma nakupatsa theka
Mwina titha ku worka ndine rapper nde ma flaws ndi ambiri
Zokangana zitha kukhala mbiri
Utha kundikonda utafuna
Nditha kukukonda nditafuna
Titha kusiyanaso titafuna
Chikondi chokha sichikwana ukakhala ma muna
Ndidziwetse
Don't just go around conners
Don't make all this about you
Tayesa zosathekaaaa
Ndisiyeee ndipiteee
Ndidziwetse
Don't just go around conners
Don't make all this about you
Tayesa zosathekaaaa
Ndisiyeee ndipiteno
Aaaaaaaaa ndisiyeee ndipite
Eeeeeee set me freee
Aaaaaaaa ndisiyaaa ndipiteeeno
Eeeeeeee set me free
Written by: Chisomo Phiri, Daniel Tadala Kasinjeni, Nathaniel Chaluchalu
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...