album cover
Atate
album cover
Atate è stato pubblicato il 1 gennaio 1977 da Now-Again Records come parte dell'album 45,000 Volts
1 gennaio 1977
EtichettaNow-Again Records
LinguaEnglish
BPM117
Melodicità
Acousticità
Valence
Ballabilità
Energia

Testi

Popita ku nchito a ibala to siya
Ndalama ya chakudya pa nyumba
Ngati ba choka ku nchito
Ba pitila to bar
Balezela moba wa 10 kwacha
Pobwela ku nyumba ati iwe mukazi wanga
Nipase vi nsima na vi ndiyo
Amai nabo ati imwe mulibe ku siya ndalama ya chakudya pano pa nyumba
Atete iwo a yamba to kalipa
Avula ma jacket ati nizaku lungiza iwe
A-a-atate lekani kumenyana ndi akazi atu
A-a-atate lekani kumenyana ndi amai atu
A-a-atate lekani kumenyana ndi amai atu
Please atate lekani ku chita ndeu
Ine sindifuna ku menya amai anga
Popita ku nchita mosaibala ku siya
Ndalama ya chakudya pa nyumba
Chifukwa ntau ina ana onse
Azankala ndi njala pano pa nyumba
Amai nabo akati ayanguleko imwe mwa yamba ku bachita ndeu
A-a-atate lekani kumenyana ndi amai atu
A-a-atate lekani kumenyana ndi amai atu
A-a-atate lekani kumenyana ndi amai atu
A-a-atate lekani kumenyana ndi amai atu
A-a-atate lekani kumenyana ndi amai atu
A-a-atate lekani kumenyana ndi amai atu
Written by: Chrissy Zebby Tembo, Paul Ngozi, Tommy Mwale
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...