album cover
Lessons (Intro)
183
Hip-Hop/Rap
Lessons (Intro) è stato pubblicato il 4 febbraio 2022 da 3767216 Records DK come parte dell'album Le$$On$
album cover
AlbumLe$$On$
Data di uscita4 febbraio 2022
Etichetta3767216 Records DK
Melodicità
Acousticità
Valence
Ballabilità
Energia
BPM87

Crediti

COMPOSITION & LYRICS
Evans Chimwala
Evans Chimwala
Songwriter

Testi

My, my name is EvanzMuzik
And I'm uh, a hip hop story teller
Listen
Chaka chino ndungofuna kusintha mindset yanga
Ambiri ndiwatuluka ndisintha number yanga
Ndufuna ndidzipatse chinthawi chodzitolera
Pali zinthu zingapo ndimafuna nditagela
Chaka chino ndufuna ndiphuzire kudziletsa
Ndidzingowapewa anthu ofuna kundiyesa
Ndiphunzire kufuna kudziwa, mkudzichepetsa
Ndiphunzire kulimbikira osati macheza
Ndikufuna ndiphunzire kumangopanga zanga
Ndiphunzire kukana kukamba nkhani yoti siyanga
Ndiphunzire kutsogoza Mulungu pa chilichonse ndikupanga
Ndikufuna kuphunzira kumakhululuka nsanga
Makamaka ndikufuna ndiphuzire kupemphera
Ndiphuzire kupitiliza pomwe ndikulephera
Ndiphunzire, kusunga zinsinsi pa society
Ndiphunzire zambiri za servitude ndi loyalty
Ndikufuna Ndiphunzire kukhala sober
Ndiphunzire kupilira akazanditchula zoba
Topic ya zachikondi chonde gaireni notes
Ndukufuna Ndiphunzire kukhala ndi mkazi m'modzi
Ndiphunzitseni, ndiphunzitseni
Ndiphunzitseni, ndiphunzitseni
Ndiphunzitseni, ndiphunzitseni
Ndiphunzitseni, ndiphunzitseni
Ndiphunzitseni, ndiphunzitseni
Written by: Evans Chimwala
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...