Testi

Mwana wanga Ngati umandikonda mvetsela Mwana wanga ngati umaukonda moyo wako sintha Mwana wanga Ngati umandikonda mvetsela Mwana wanga ngati umaukonda moyo wako sintha Ndati palibe palibe palibe Angakugwile dzanja pamavuto Ndati palibe palibe palibe Angakugwile dzanja pamavuto mwanawe Kamdothi thawa mvula Kamdothi thawa mvula Kamdothi thawa mvula Kamdothi thawa mvula Kamdothi thawa mvula Uuuuh mwana wanga mvetsela mvetsela Uuuuh mwana wanga mvetsela mvetsela Komabe njoya mosamala poti nkhondo ndi anansi Amabwela ngati achibale koma mpeni atapanila kuphanzi Komabe njoya mosamala poti nkhondo ndi anansi Amabwela ngati achibale koma mpeni atapanila kuphanzi Uuuuh mwana wanga mvetsela, mvetsela Uuuuh mwana wanga mvetsela, mvetsela Komabe njoya mosamala poti nkhondo ndi anansi Amabwela ngati achibale koma mpeni atapanila kuphanzi Komabe njoya mosamala poti nkhondo ndi anansi Amabwela ngati achibale koma mpeni atapanila kuphanzi
Writer(s): Robert Ching'amba Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out