album cover
Bisa
album cover
Bisa è stato pubblicato il 3 dicembre 2022 da Malawi Goodlife come parte dell'album LOVE & HATE (The 20th and Final Release)
3 dicembre 2022
EtichettaMalawi Goodlife
LinguaEnglish
BPM173
Melodicità
Acousticità
Valence
Ballabilità
Energia

Testi

Bisa bisa bisa bisa bisa
Udzawulure zikadzatheka
Tiuze mungokhala chete bisa
Adzangowona zikadzayenda
Pakuti dziko linayipa
Ladzadza afisi ndi mibulu ya jealous
Udzingosunga mu mtima mwako
Adzingodziwa Mbuye yekha, wakumwamba
Uzingokomela anzako
Koma usamangomvera zilizonse
Si onse ukucheza nawo amakukonda
Abwenzi lero mawa adani
Samangokhulupira onse
Yemweyo ukudya nayeyo adzakupeleke
Kaya ufuna kugula nyumba
Adzangowona ukadzagula
Ngati ufuna kugula galimoto
Adzangowona ukuwa waver
Kaya wapeza wako
Ufuna kumanga banja
Adzangowonera pa wedding card
Usamalengeze zinthu zilizonse
Umampatsa mpata Satana
Zimkayenda bwino kale
Pomwe amkadya kachetechete
Samkapitapita kumudzi
Moyo wake udali wamphamvu
Ana kubala apite kumudzi
Wakaputa mavu pachisa
Chonsecho adawatengera katundu wankhaninkhani
Adawatengeranso ndalama
Bisa bisa bisa bisa bisa
Udzawulure zikadzatheka
Tiuze mungokhala chete bisa
Adzangowona zikadzayenda
Pakuti dziko linayipa
Ladzadza afisi ndi mibulu ya jealous
Udzingosunga mu mtima mwako
Adzingodziwa Mbuye yekha, wakumwamba
Uzingokomela anzako
Koma usamangomvera zilizonse
Si onse ukucheza nawo amakukonda
Abwenzi lero mawa adani
Samangokhulupira onse
Yemweyo ukudya nayeyo adzakupeleke
Chinali chibwenzi chobeba
Amkangocheza mwachinsisi
Adamuchemelera pagulu
Kuti bwezi lake ndi wachuma
Sanadziwe kuti anzake amkasilira
Zinthu zayamba kuvuta
Lero sakuyankha phone
Sakuyankha message
Mwapeleka momwetamweta
Bisa bisa bisa bisa bisa
Udzawulure zikadzatheka
Tiuze mungokhala chete bisa
Adzangowona zikadzayenda
Pakuti dziko linayipa
Ladzadza afisi ndi mibulu ya jealous
Udzingosunga mu mtima mwako
Adzingodziwa Mbuye yekha, wakumwamba
Uzingokomela anzako
Koma usamangomvera zilizonse
Si onse ukucheza nawo amakukonda
Abwenzi lero mawa adani
Samangokhulupira onse
Yemweyo ukudya nayeyo adzakupeleke
Written by: Lucius Banda
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...