Crediti
COMPOSITION & LYRICS
Yobe Gweula Phiri
Songwriter
Precious Orama Ngwende
Songwriter
Emmanuel Moyo
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Mystery the Beat King Kong
Producer
Madela
Mastering Engineer
Testi
Classic
Mmm-mm… Orama
Yobezani
Eeeh
Emmanuel, yeah
Eeeh! akandiwona
N'takhumudwa n'sakukondwa
Kumakondwera iwowa
Kumandijeda iwowa
Eeeh! Mbuye wanga ndi Mtondo, ndi Mtondo, ndi Mtondo
Tate wanga ndi Leader, ndi leader, ndi Leader
Tate wanga ndi Leader
Ndipo sindidzalira
Ndithu sadzandisiya
Ine ndikuyamika
Yeah, I gotta be honest
Siwina koma Inuyo
Sin'zitengera chizolowezi
I owe it all to You, Lord
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Ndilibe chifukwa chodzitamira
'Cause I know I'm just a product of Your Grace
Chipanda Inu bwezi nditataika
No doubt, yeah I coulda been some waste
N'nalawa ubwino Wanu
Munandigula ndi mwazi n'kundipanga Wanu
Munandipatsa moyo wina, now I'm brand new
And I'm enjoying its fullness, sorry Dan Lu
Yeah! I acknowledge it's all You, Lord
M'mene n'nali mu dead-end munali clue, Lord
Ndikupanga self-searching munali Google
Till I found myself engulfed in Your cool Love
Ngiyabonga
Yeah, I gotta be honest
Siwina koma Inuyo
Sin'zitengera chizolowezi
I owe it all to You, Lord
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Kundiombola m'zikhomo
Adani anatseka, mwanditsegulira khomo
Nkhawa n'napachika ndimayenda mu zisomo
Ndi Yesu zonse zinayera n'mwazi osati Omo
Zomwe mwachita pa moyo wanga indedi n'zambirimbiri
Mwakuza malire anga, ndikundisinthanso mbiri
Adani kundipinga n'cholinga choti andikole mu goli
Koma munandi-saver m'manja mwawo, munawayika zigoli
Ndadza pano kunena zikomo
Mdalitso Wanu umabweretsa bata m'timamo
Sindikulabada olo dyabu akoke tsinya
Chomwe ndikuchita nkhumupokera Chiuta wa ku chanya
Yeah, I gotta be honest
Siwina koma Inuyo
Sin'zitengera chizolowezi
I owe it all to You, Lord
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Written by: Emmanuel Moyo, Precious Orama Ngwende, Yobe Gweula Phiri

