album cover
MADA
427
Hip-Hop/Rap
MADA è stato pubblicato il 5 marzo 2024 da It's Only Entertainment come parte dell'album MADA - Single
album cover
Data di uscita5 marzo 2024
EtichettaIt's Only Entertainment
Melodicità
Acousticità
Valence
Ballabilità
Energia
BPM113

Testi

Yeah
It's Only Entertainment
Very Good Very Good
Sameface on the Beats
Mumakwana a Mada
Mwabhebha mwabhebha
Mwaipatsa moto a Mada
Mwatentha mwatentha
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Amati akanyamuka ndi ma baddie
Akupita ku mango talati
Akachoka pamenepo restaurant
Kenako ku zi ma photo kwa stunt
Popita ku dance savala panti
Kuti mphepo idutse bwino pati
Amakonda nyama mu chapati
Ngati kuli kobhebha ali mkati
Ali ndi chi latest iPhone
Akundivutitsanso ndimugulire Benz
Akumangojomba daily class
Akudziwa kuti lecturer adya beans
Why you gotta do me like this? Mada
Ukufuna kuti ndipange commit murder?
Ukupanga chani Madalitso
Funa khoba izawatenge Fada?
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Kumupempha kuti abweze ko moto wakana
Ati palibe zopola
Ukamuonaa akubalalitsa
Panopo nde zinamuyanja zodzola
Wachita kumenyetsa nkhwangwa pa mwala
Kuti iyeyo ndi loan ndi wokongola
Ukaona pa watch ndi nthawi yake
Yamukwanira ndendende yonjoya
Akumandikanda pa bala
Kunyamuka kwawo kumakadukula ku Bala
Nsanje zochita kuputa dala
Kuti ine ndizikangana ndi midala
Why you gotta do me like this? Mada
Ukufuna kuti ndipange commit murder?
Ukupanga chani Madalitso
Funa khoba izawatenge Fada?
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Cuff-B Production
Written by: Noel Phyzix Chikoleka
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...