album cover
Mtendere
African
Mtendere è stato pubblicato il 6 gennaio 2026 da Mwankisi come parte dell'album Mtendere - Single
album cover
Data di uscita6 gennaio 2026
EtichettaMwankisi
LanguageEnglish
Melodicità
Acousticità
Valence
Ballabilità
Energia
BPM80

Crediti

PERFORMING ARTISTS
Mwankisi
Mwankisi
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Ntulitutule Matandala
Ntulitutule Matandala
Composer

Testi

Tikufuna mtendere inu mutivele
Akufuna ntchito inu muwalembe
Anatifera John Chilembwe
Tiyeni ndikukakhana lende
Tikufuna mtendere inu mutivele
Akufuna ntchito inu muwalembe
Anatifera John Chilembwe
Tiyeni ndikukakhana lende
Kalonga wa mtendere
Iwe si ine chindere
Yodetsa saona ndege
Tikufuna mtendere zinthu ziyende
Opanda chiphaso ndi ndende
Tiyeni miyala timugende
Anabwera anatisiyila chingende
Minda afuna atenge iwo alemele
Dzala libwerere ndi akuba tichenjele
Sukulu ya ukachenjede ndaona mayekete
Tikufuna mtendere zinthu ziyende
Kusiyana Kwa parliament ndi ndende
Si nthawi yoti so utinyenge
Chilungamo chokha nde unene
Tikufuna mtendere zinthu ziyende
Kusiyana Kwa parliament ndi ndende
Si nthawi yoti so utinyenge
Chilungamo chokha nde unene
Tikufuna mtendere inu mutivele
Akufuna ntchito inu muwalembe
Anatifera John Chilembwe
Tiyeni ndikukakhana lende
Tikufuna mtendere inu mutivele
Akufuna ntchito inu muwalembe
Anatifera John Chilembwe
Tiyeni ndikukakhana lende
Walumidwa ndi njenjete
Kusekedwa ndi aphwete
Si ndiwo ife si zipwete
Si nyama kuti uticheke
Chilungamo chioneke
Madzi atayika awoleke
Sitilora chipangano chionongeke
Babulo agwe ndi onyenga
Za anthu osowa mukutenga
Mavuto madza ngati matenda
Yo panda makhwala nsanje matenda
Tikufuna mtendere zinthu ziyende
Kusiyana Kwa parliament ndi ndende
Si nthawi yoti so utinyenge
Chilungamo chokha nde unene
Tikufuna mtendere zinthu ziyende
Kusiyana Kwa parliament ndi ndende
Si nthawi yoti so utinyenge
Chilungamo chokha nde unene
Written by: Ntulitutule Matandala
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...