album cover
SUNTHA
Hip-Hop/Rap
SUNTHA è stato pubblicato il 21 marzo 2026 da BVRELYSOBVGVNG WORLDWIDE/TURNUP MUSIC come parte dell'album SUNTHA - Single
album cover
Data di uscita21 marzo 2026
EtichettaBVRELYSOBVGVNG WORLDWIDE/TURNUP MUSIC
LanguageEnglish
Melodicità
Acousticità
Valence
Ballabilità
Energia
BPM89

Crediti

PERFORMING ARTISTS
DBturnUp
DBturnUp
Rap
COMPOSITION & LYRICS
Dearborn Chris Malindah
Dearborn Chris Malindah
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
BlackT
BlackT
Engineer

Testi

Yeah
Ey
Huh
BVRELYSOBVGVNG!
Yeah
Ey
Huh
Wooh
Bvrelysobvgvng ndife ana ofuntha
Hiphop bhobho dzulo nnali ndi pupa
Sindingamayende choncho eya nnali ndi shoota
Kudya nde tikudya koma osamakhuta
If you take it easy life simakuvuta
Sindicheza ndima bitch ndiye osandiputa
Ma move anuwo ifeyo samatisuntha
Ku baller ndi pa ground ife timaijuja
Eya timaijuja
Ofùna kuyaka nafe mawa amazaduka
Olimbana ndi ifeyoyo amayaluka
Sindingagwilikeso ineyo huh ndinaluta
Iwe turnup crown yo osaitula
About to save the city nkhani yake ya super
Ngati sizacash chonde osanditchula
Iwo aku seller dreams ife simaigula
Ha
Simaizula
Kudzala kuthilila kenaka ndi kuphuka
Bread mulibeso muthamangila kutchuka
Imeneyo si growth Mwina mwake chotupa
Pano mmangowadusa
Anawa ndi oyela ifeyo timawauser
Kuti nzipanga udolo Ine ndinangofuna
Ngati radio ma frequencies ndimangotuner
Ma mission ndima runner ine osandifusa
Ulemu kwa akazi omwe amandifuna
Ndine trap minister Ena Ati ndi nduna
Maguy muli mmadzi mungocheza ndi mbuna
Guess it's coming quiet sooner
Dollar ndi zambiri ngati timasandusa
We be cutting **** off ngati timajandusa
Ngini yathu ili in motion ife tinayibandusa
Pepani tu tadusa
Kodi nanga bwanji DBturnUp walusa
Ndawaona ana ambili kuti akumapusa
Aneneli onyengawo ife timawasusa
Hie Mr hater it is nice to meet you
I'm just steady hoping that this vibe will reach you
You could resonate and maybe that will teach ya
That love is the drug that will die here withchu
Written by: Dearborn Chris Malindah
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...