album cover
Limodzi
album cover
00:00
01:00
01:05
01:15
03:40
00:00
03:52
Ultimi 7 giorni
Limodzi è stata scoperta più frequentemente a circa 1 minuti and 5 secondi dall'inizio la canzone durante la settimana passata

Testi

265 got the sauce in here
Mm, hmm-hmm, mm
Oh-oh-oh
Oh-oh-oh
Oh-oh-oh
Ikonini-nini
Ukanditenga bwino uzadya nane
Uzadya nane, uzadya nane
Ukanditenga bwino uzadya nane
Uzadya nane (Aight), uzadya nane (Oh)
Ukanditenga bwino uzadya nane
Uzadya nane, uzadya nane
Ukanditenga bwino uzadya nane
Uzadya nane, uzadya nane
Kuyendera limodzi, kulemera limodzi
Kudyelera limodzi, kulikonse limodzi
Kuyendera limodzi, kulemera limodzi (Ayo, Tiyeni)
Kudyelera limodzi, kulikonse limodzi (Tiyeni, Tiyeni, Tiyeni, eish)
Mm, zaka zapitazo ine osanama sindinali mene ndililimu, ndililimu
Zaka zapitazo ine osanama sindinali mene ndililimu, ndililimu
Koma Unanditenga, kundisamalira lero ndine chidhilu, chidhilu
Unanditenga kundisamaliralero ndine chidhilu, ndine chidhilu
Talemela limodzi, tiyendele limodzi, tinjoyele limodzi, limodzi
Talemela limodzi, tiyendele limodzi, tinjoyele limodzi (Ah)
Ukanditenga bwino uzadya nane
Uzadya nane, uzadya nane
Ukanditenga bwino uzadya nane
Uzadya nane (Aight), uzadya nane
Ukanditenga bwino uzadya nane
Uzadya nane, uzadya nane
Ukanditenga bwino uzadya nane
Uzadya nane, uzadya nane
Kuyendera limodzi, kulemera limodzi
Kudyelera limodzi, kulikonse limodzi
Kuyendera limodzi, kulemera limodzi
Kudyelera limodzi, kulikonse limodzi
Ukanditenga bwino uzadya nane
Uzadya nane, uzadya nane
Eh, eh, eh, eh, eh (Ah-ah)
(Uzadya nane) 50 Billion
(Uzadya nane) Tazipeza
Ah-ah, eh
Ah-ah, eh
Ah-ah
Written by: Joe Ikon, Zeze Kingston
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...