Testi

Panali anthu ena wongovutika Pamene anthu ena amkangokondwera Panalia anthu ena wogwira ntchito Pamene anthu ena amkangodyelera Malume ndalama kubisa ku bank Pamene mbumba yanu ikufa ndi njala Koma zowuluka zonse zitawuluka Pali tsiku limodzi zitadzatele Inu mumati zidzakhala choncho Mpaka liti abale? Ana a Mulungu sangakhale akulira Masiku onse a moyo wawo Analanda ufumu kalero Nawupeleka kwa woyenera Ndichani chingamulake Mbuye Mulungu wachilungamo! Ndi wachikondi Tsiku la Mulungu ndi lopambana Koma linali tsiku la masewera Amayi kulephera kusunga banja Koma Ambuye sanakondwere nazo Anthu anzeru opempha chilungamo Amkangofa monga muja zifera ntchetche Koma zowuluka zonse zitawuluka Pali tsiku limodzi zitadzatele Inu mumati zidzakhala choncho Mpaka liti abale? Ana a Mulungu sangakhale akulira Masiku onse a moyo wawo Analanda ufumu kalero Nawupeleka kwa woyenera Ndichani chingamulake Mbuye Mulungu wachilungamo! Ndi wachikondi Ukhululuke iwe nzanga ofedwa Puputa misozi tiyiwale zonse Nyali yawala nkhuku ija yathawa Tisangalare poti Mbuye watikumbuka Zokulipa diso izo siyani Zikanatero bwezi tonse tili a khungu Kukhululuka ndiye ndakhululuka Koma mabalawa ndiye akupweteka Inu mumati zidzakhala choncho Mpaka liti abale? Ana a Mulungu sangakhale akulira Masiku onse a moyo wawo Analanda ufumu kalero Nawupeleka kwa woyenera Ndichani chingamulake Mbuye Mulungu wachilungamo! Inu mumati zidzakhala choncho Mpaka liti abale? Ana a Mulungu sangakhale akulira Masiku onse a moyo wawo Analanda ufumu kalero Nawupeleka kwa woyenera Ndichani chingamulake Mbuye Mulungu wachilungamo! Inu mumati zidzakhala choncho Mpaka liti abale? Ana a Mulungu sangakhale akulira Masiku onse a moyo wawo Analanda ufumu kalero Nawupeleka kwa woyenera Ndichani chingamulake Mbuye Mulungu wachilungamo! Inu mumati zidzakhala choncho Mpaka liti abale? Ana a Mulungu sangakhale akulira Masiku onse a moyo wawo
Writer(s): Lucius Banda Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out