album cover
Athaima
album cover
Athaima è stato pubblicato il 12 giugno 2026 da It's Only Entertainment come parte dell'album Mphungu
AlbumMphungu
12 giugno 2026
EtichettaIt's Only Entertainment
LinguaEnglish
BPM91
Melodicità
Acousticità
Valence
Ballabilità
Energia

Video musicale

Video musicale

Testi

(Mphungu screeching)
It's Only Entertainment
Tonicity
Nyimbo zanga zonse ndi za lit
This is This is This is
Unaimbako hit liti?
Yeah
Very Good Very Good
This is album number seventeen
Addicted to rap ngati muli nicotine
Tapanga za ma hit from the time I was a teen
Kukonda kugawa makofiku nkusaka caffeine
Not a regular rapper this is a rare breed
Anthu oti sitimakonda kuluza you don't beat
How are you gonna face me yet you a deadbeat
I'm the father of rap ndimaphaso ma beat
Yodelera dolo ndiiti yiti
Taona chi mkazi titty titty
Ndili ndi chi show gula tikiti
USAJOMBE zatenge tpt
Akamathoka ngati mwano
Akamakamba ngati nthano
Ngati kuti si pompano
Zachibwana ayitu this I know
Samathaima
Pano athaima
Samadziwa pano adziwa
Samathaima
Pano athaima
Zachibwana ayitu this I know
This is album number seventeen
Timavala ankle boot pano Christian Louboutin
Tikagwira mkazi anali achina abiti Jane
Panopo kungondiyakila be a solid 10
Zomwe ife timapanga is for the win
I'm not regular person a celestial seraphin
Mafanawa ndi ma chaser I am the gin
Kulimbana ndi mwini filimu it's a bloody scene
Yodelera dolo ndiiti yiti
Taona chi mkazi titty titty
Ndili ndi chi show gula tikiti
USAJOMBE zatenge tpt
Akamathoka ngati mwano
Akamakamba ngati nthano
Ngati kuti si pompano
Zachibwana ayitu this I know
Samathaima
Pano athaima
Samadziwa pano adziwa
Samathaima
Pano athaima
Zachibwana ayitu this I know
Unaimbako hit liti?
Written by: Noel Phyzix Chikoleka
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...