album cover
Mulimi
album cover
Mulimi è stato pubblicato il 20 maggio 2026 da SLEYAN ESSENTIALS come parte dell'album LOI
AlbumLOI
20 maggio 2026
EtichettaSLEYAN ESSENTIALS
LinguaEnglish
BPM81
Melodicità
Acousticità
Valence
Ballabilità
Energia

Video musicale

Video musicale

Testi

Mlimi akadzala mbeeu saifukula
Ayithilila nayang'anila sakumba kuti aoone
Mmene ikukila
Amathila manyowa nalindila mvula
Ndipo mbeeu ikamela mulimi asangalala
Podziwa thukutalache silinapite pachabe
Ndipo aka kolola adya ndibanja lake
Zikachuluka zima agulitsa
Khala ndi patience ngati mulimi
Dzala ngati mulimi
Thilila ngati mulimi
Palila ngati mulimi yeee
Dikila ngati mulimi nupemphela ngati mulimi
Ndipo udzakolola
Ukalimbikula,sudzasowa kanthu ndipo mbiliyako idzamveka kuma area kumbukila mau anena udzadya thukuta lako yehova adza dalitsa ntchito zamanja ako ndipo mbeeu ikamela
Mulimi asangalala podziwa thukutalako silinapite pachabe
Khala ndi patience ngati mulimi
Dzala ngati mulimi
Thilila ngati mulimi
Palila ngati mulimi yeee
Dikila ngati mulimi nupemphela ngati mulimi
Ndipo udzakolola
Written by: loiswayo alvin roben
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...