album cover
Tcheka
album cover
Tcheka è stato pubblicato il 10 novembre 2026 da Deebo Creatives come parte dell'album Tcheka - Single
Data di uscita10 novembre 2026
EtichettaDeebo Creatives
BPM122
Melodicità
Acousticità
Valence
Ballabilità
Energia

Testi

Zinayamba ngati zocheza, pano zafika pokoma, ine ndikamuyang’ana wangayu
kukhala ngati ndikulota.
Ena ankanditemberela, amkati sindidzamupeza koma pano akusowa zokamba mdalitso wachoka kumwamba.
Mundilole ndimukonderetu zamawa sizidziwika,
chikondi ndimupatsiretu poti ndamusankha ndekha
Ona chisankho cha ine _ Tcheka Tcheka
Tcheka chi bea chaine _ Tcheka Tcheka
Nde chikamayenda_ Tcheka Tcheka
Chikati chiime apooo_ Tcheka Tcheka
Umu muli chi vibe _ Tcheka Tcheka
Type yanga ndi iyiyi ish! Tcheka Tcheka
Izizi siza sewero, ine ndikakonda munthu ndimapereka mtima wanga onse!
Ndiye bola ndineneretu lero oh!
usamaganize zolekana ndine.
Ndie asatana nonse lero mukunama!sizingatheke kudzatilekanitsa,
ndipo
sindingalole kukamuyamba wina no!
muvomeleze uyu yekha ndi wanga, waanga!!
Mundilole ndimukonderetu zamawa sizidziwika,
chikondi ndimupatsiretu poti ndamusankha ndekha x2
Ona chisankho cha ine _ Tcheka Tcheka
Tcheka chi bea chaine _ Tcheka Tcheka X2
Nde chikamayenda_ Tcheka Tcheka
Chikati chiime apooo_ Tcheka Tcheka
Umu muli chi vibe _ Tcheka Tcheka
Type yanga ndi iyiyi ish! Tcheka Tcheka

Loading...