クレジット
PERFORMING ARTISTS
Mr Blaq Eti
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Jacob Mwanza
Songwriter
Kings Siwakwi
Songwriter
歌詞
Yeah I'm Mr Blaq Eti yeah
Mmani konda neh mwani konda neh
Naona ambuye mmani konda neh
Pazomwe muma chita nkuti zikomo baba baba
Yeah ambuye amandi kondela neh
Ndiye cifukwa niyendela mokondwela neh
Madaliso ndi ambili nisowa mopendela ndiye
Apa nikuzinva nga ndine free Mandela yeah
Stacking up madaliso stacking up
Pakilako nayo yango pakilako
Samandi lekelela ambuye never backing out
Ngati ufuna kundiyesa tiye choka out
Amandi nthandiza pama vuto
Could have failed koma anati iyo sivuto
Pasa mwana wanga koma next time do better
Nde chino chaka neh nabwela as a goal getter
So ndikuti
Pandithandidza ambuye ineyo
Even when I feel I don't deserve it nthawi zina
Mmani konda neh mwani konda neh
Naona ambuye mmani konda neh
Pazomwe muma chita nkuti zikomo baba
Mmani konda neh mwani konda neh
Naona ambuye mmani konda neh
Pazomwe muma chita nkuti zikomo baba
Ine chiuta oni temwa chomene and I've seen it yeah
Masuzgo nayaleka pa seen
Not pure nkhumanya kanandi ine I sin
Elo Chalo chili hard chomene ngan jean
Truth is nyengo zinyake abale ine nkhulila
Mbwe luta kwa chiuta mukulila
Chalo ichi nchinonono
Kwe kwa chiuta NoNo
Vuto langa sivuto olo pang'ono
So nkhumu ongani adada pa ivi munichitila neh
Panekha ivi vukuni kulila neh
Muli na ine ndimwe vyose vibenge makola
Mudangilila woko yane mulikola
Nikuti zikomo pazomwe mumachita baba
Ine naona chisomo mumoyo wanga mumoyo wanga
Nikuti zikomo pazomwe mumachita baba
Ine naona chisomo mumoyo wanga mumoyo wanga
Mmani konda neh mwani konda neh
Naona ambuye mmani konda neh
Pazomwe muma chita nkuti zikomo baba
Mmani konda neh mwani konda neh
Naona ambuye mmani konda neh
Pazomwe muma chita nkuti zikomo baba
Nikuti zikomo pazomwe mumachita baba
Ine naona chisomo mumoyo wanga mumoyo wanga
Nikuti zikomo pazomwe mumachita baba
Ine naona chisomo mumoyo wanga mumoyo wanga
Written by: Jacob Mwanza, Kings Siwakwi