クレジット
COMPOSITION & LYRICS
Daniel Tadala Kasinjeni
Songwriter
Duncan Zgambo
Songwriter
Temwah Gondwe
Songwriter
Francis Kaphuka
Songwriter
歌詞
I'm going to be a singer
Aaaah a superstar
And a doctor and a dentist
Superstar Superstar Superstar
Kuwala nyenyezi mam'mawa
One day
Cause I wanna be a superstar
Heheee Yooh
Kutsegula TV Hyphen radio Hyphen
Koma a Malawi azamvelako nyimbo za ife?
Kuphusha ndikuphusha koma ngini ingonjanja
Fame sitiyanja madalitso si nyanja
Ndikufuna kutchuka mwina nkugula ka Demio
Munthune ndikukula nchoke den ya masten yo
Kuyang'ana FB ndione ngati anankambako
Koma kuti ndi trende ndimenye yanga anankabango
Koma kuphusha tingophusha sizutheka
Nyimbo zathu zogontha sizumveka
Ine nditani mulungu ngapange bwanji
Funa kutchuka ka ndikhale superstar
Ndili ndimaloto ambiri koma sindikugona
Ndimalimbikila nokha mutha kuona
Ndimakhala ndi mantha
Sizipezeka kuti nthawi yanga yatha
I wanna be a superstar
(Superstar superstar)
Cause I wanna be a superstar
(Superstar superstar)
Keep on chasing your dreams
All the times
Kumalimbikila kumaikapo mtima ndipo udzakhala superstar
(Superstar superstar)
Hey Look!
Njira yake siyophweka umayamba ndikusochela
Kwina nkulimbika kwakukulu nkukondeledwa
Zitseko kutsekedwa osalephela opondeleza
Speak highly of yourself poti mau amalosera
Kuona komwe tachokela zoti ife tinkasekedwa
Nkanamvela bwezi loto titamezedwa
So I show up and I show out zonse zinalembedwa
Khama ndi maso mphenya pano ma level ndi ena
See you gonna feel it in you when you're chosen
Pano tinakhazikika mu game kumanga mudzi ngati goshen
I've seen doors open malo omwe tinkapempha kuti tikondeni
Heavy is the head, and it came to life everything that I've ever spoken
Don't let your spirit be broken
Ndili ndimaloto ambiri koma sindikugona
Ndimalimbikila nokha mutha kuona
Ndimakhala ndi mantha
Cause I wanna be a superstar
(Superstar superstar)
Cause I wanna be a superstar
(Superstar superstar)
Keep on chasing your dreams
All the times
Kumalimbikila kumaikapo mtima ndipo udzakhala superstar
(Superstar superstar)
Written by: Daniel Tadala Kasinjeni, Duncan Zgambo, Francis Kaphuka, Temwah Gondwe