ミュージックビデオ
ミュージックビデオ
クレジット
PERFORMING ARTISTS
Malinga
Vocals
Malaika "Lady Aika" Chikalimba
Background Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Chikumbutso Chitsundi Banda
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Sickle Dj Sley Sapa
Producer
歌詞
Mmmmmh
Yeah Yeah
Dj Sley
Ngati afuna tizikangana
Auzeni kuti nthawi ndilibe
Ngati afuna tizimenyana
Awina mphamvu ndilibe
Ndilibe
Ndilibe
Awina mphamvu ndilibe
Ine ndimajama yanga
Kuthamangitsa hustle yanga
My own lane own pace
Musandipatse phuma zanu zikatheka nsanga
I am here to fight poverty
Buy alot of property
Sikuti mwakati
Mumie knows great man I wanna be
Gimme di light me wanna burn some carna B
Uptown deh so me waan me mama live
Make hits tour the world like Burna B
Me want it all not just part of it
Ngati afuna tizikangana
Auzeni kuti nthawi ndilibe
Ngati afuna tizimenyana
Awina mphamvu ndilibe
Ndilibe
Ndilibe
Awina mphamvu ndilibe
Ndimakhala kusaka chuma
Ndipo ndilibe phuma
Mvula ikagwa kumauma
That's why me gas it up ngati Puma
Yute fight poverty not another man
Hits we a pree Sley drop another one
Born leader true me no follow man
Yute affi wise up King Solomon
That's why that's why
Me work so hard fi what's mine
Badmind atha kuika landmine
Red eye love your madda 10 time
Badmind
Ngati afuna tizikangana
Auzeni kuti nthawi ndilibe
Ngati afuna tizimenyana
Awina mphamvu ndilibe
Ndilibe
Ndilibe
Awina mphamvu ndilibe
Ngati afuna tizikangana
Auzeni kuti nthawi ndilibe
Ngati afuna tizimenyana
Awina mphamvu ndilibe
Ndilibe
Ndilibe
Ndilibe
Ndilibe
Ndilibe
Awina mphamvu ndilibe
Ndilibe Ndilibe Ndilibe
Awina mphamvu ndilibe
Written by: Chikumbutso Chitsundi Banda