ミュージックビデオ

ミュージックビデオ

クレジット

PERFORMING ARTISTS
Emmie Deebo
Emmie Deebo
Background Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Emily Zintambira
Emily Zintambira
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Chawa Beatz
Chawa Beatz
Producer

歌詞

Naaa Naaa Naaah
Naaa Naaa Naaah
Eyo! tiyeni! Deebo
Tiyeni tiyeni tiyeni, Eish!
Lelo lokha situkasaka ndalama
Lelo lokha sitilimbana ndi munthu
Lelo lokha social media palibe eh!
Lelo lokha sitilimbana ndi munthu
Eyooo oooh! Ifeyo tufuna timasuke
Eyooo oooh! No ma stress ife timasuke
Tizipepese (patse space)
Tizipumitse(usandisokoneze)
Tisangalale, tifile mpaka kuche
Tizipepese (patse space)
Tizipumitse(usandisokoneze)
Tisangalala, tifile mpaka kuche
Ati, bwanji mukubwela maso ali gwa
Ngati chomwe ndikupanga sindikudziwayi
Esh, basi kufuna kuwoneka odziwa
Kodi momwe ndimavutika inu munali kwani?
Lelo ndapeza zokwana ndapeza zokwana
Ndapeza ah! zokwana, I'm a champion
Lelo ndapeza zokwana ndapeza zokwana
Ndapeza ah! zokwana, I'm a champion
Tizipepese (patse space)
Tizipumitse(usandisokoneze)
Tisangalale, tifile mpaka kuche
Tizipepese (patse space)
tizipumitse(usandisokoneze)
tisangalala, tifile mpaka kuche
Tizipepese (patse space)
Usandisokoneze
Tisangalala, tifile mpaka kuche
Tizipepese (patse space)
Tizipumitse(usandisokoneze)
Tisangalala, tifile mpaka kuche
Naaa Naaa Naaah
Naaa Naaa Naaah
Tizipepese (patse space)
Tizipumitse(usandisokoneze)
Tisangalala, tifile mpaka kuche
Written by: Emily Zintambira
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...