크레딧
작곡 및 작사
Bright Michael Mitumbiri
작사가 겸 작곡가
Allster Momba
작사가 겸 작곡가
Samuel Nsauka
작사가 겸 작곡가
Martin
작사가 겸 작곡가
가사
When you tell the truth justice is done but lies lead to injustice
Oops on the board
Mick Wizz on the beat
Simukunamiza ife mukuzinamiza nokha
Oowo
Zomwe mumapanga ambuye amaona
Oowo owoo
Ambuye amaona ambuye samagona
Simukunamiza ife mukuzinamiza nokha
Oowo
Zomwe mumapanga ambuye amaona
Oowo owoo
Ambuye amaona ambuye samagona aa aaa
Ndiya boza chabe ndima church goer
Amanamizila zamulungu mawa aliku mowa
Chi Christu chawo basi ndi chizolowezi
Ukawafutsa amakuwuza ndingonjoya wezi
Maka maka auntwa akaona benz
Amangolola aliyese bolani chibwezi
Asaone dona braz kuthamanga mwazi
Kuzolowela uchimo kunamiza akazi
Kuyiwala yesu nkhristu anawakhesela mwazi
Nzeru yasatana ija akuyimva kukoma
Yawo syllabus kupanga zauchimo basi
Njila zawo zamun'dima akusata wawo ntima
Kupangila dala mu church anangobisala
Kupangila dala mu church anangobisala oooh
Yehovah zonse akuona saozela samagona
Saozela samagonaaa
Simukunamiza ife mukuzinamiza nokha
Oowo
Zomwe mumapanga ambuye amaona
Oowo owoo
Ambuye amaona ambuye samagona
Simukunamiza ife mukuzinamiza nokha
Oowo
Zomwe mumapanga ambuye amaona
Oowo owoo
Ambuye amaona ambuye samagona aa aaa
Mulungu amakhululuka atenga chizolowezi
Akamapemphela ngati oyera ntima
Kale kale nkati mwawo nyale inazima
Ulaliki kwaiwo nthano koma uchimo
Kupembedza mafano
Mbale usalole devil akugwilitse ntchito
Poti ndilopwetekatu ilo lake dziko
Pembeza mulungu muudzimu ndichoona
Lapa machimo panga machawi
Popeza yesu zonsezi akuona
Yesu akubwera i mean around the corner
Usasate zathupi zilako lako
Zomwe ukupangazo sikuchenjela
Simukunamiza ife mukuzinamiza nokha
Oowo
Zomwe mumapanga ambuye amaona
Oowo owoo
Ambuye amaona ambuye samagona
Simukunamiza ife mukuzinamiza nokha
Oowo
Zomwe mumapanga ambuye amaona
Oowo owoo
Ambuye amaona ambuye samagona aa aaa
Mukuzinamiza nokha
Oowo oowo owoo
Mukuzinamiza nokha
Ooowo oowo owoo
Written by: Allster Momba, Bright Michael Mitumbiri, Martin, Samuel Nsauka

