뮤직 비디오
뮤직 비디오
크레딧
실연 아티스트
Shano Index
보컬
Tawanda Mpando
보컬
작곡 및 작사
Shano Index
작사가 겸 작곡가
Tawanda Mpando
작사가 겸 작곡가
Robert Abraham Malinga
작사가 겸 작곡가
Patrick Manyozo
작사가 겸 작곡가
프로덕션 및 엔지니어링
Robert Abraham Malinga
프로듀서
Patrick Manyozo
엔지니어
Swisha
프로듀서
가사
Ndinene motani
Ndi nene mota
Kuti zimveke
Mveke
Mveke
Mveke
Mveke
Ndinene motani
Kuti zimveke
Mveke
Mveke
Mveke
Mveke
Kuti zimveke
Kapena ndikuwe
Kapena ndikuwe
Kapena ndikuwe
Kuti zimveke
Kapena ndikuwe
Kapena ndikuwe
Kapena ndikuwe
Moni ku stand
Muli bho, muli njibwa
Ndabwera ndi ka ninkha
Mwina mwakamva kale
Nsungwana wokondedwa
Amakhala fupi mpa Chipeta paja
Wandipatsa katheka, mtima mwake zatheka
Chikondi changachi chopanda malile
Sindingatsinzine, sindingaphethile
Tatenga nkono wanga, ndiyandikile
Ndizathu zonse izizi
Dear my friend tamvelako story
I know you're busy but I'm not funny
Nkhani ndyambeta ija panopa ndi namwali wanga
Ndunenapano ndufuna ndimveke velo yowala
Everyday ine eh, mmaso mwa ine
Dzuwa lika tuluka ndimawona iye
Anakonda ine, ine nakonda iye eh
Pena mtima umagunda umagundila iye
Chikondi changachi chopanda malile
Sindingatsinzine, sindingaphethile
Tatenga nkono wanga, ndiyandikile
Ndizathu zonse izizi.
Written by: Patrick Manyozo, Robert Abraham Malinga, Shano Index, Tawanda Mpando


