album cover
Oneni
1,902
Afro-Beat
Oneni은(는) {albumName} 앨범에 수록된 곡으로 2025년 5월 22일일에 Madness Entertainment에서 발매되었습니다.Oneni - Single
album cover
발매일2025년 5월 22일
라벨Madness Entertainment
언어English
멜로디에 강한 음악
어쿠스틱 악기 중심
발랑스
춤추기 좋은 음악
에너지
BPM111

가사

Eya, yayayaya
Eya, yayayaya
Eya, yayayaya
265, Ayo Billy
Hmm, mh
Talitalitali tala
Ikon tafika no ID chinzika
Ikon tafika no ID chinzika
Mundikumbukire Atate
Mafuna ntayiphula nane
Mene mudalitsa enawa
Msandipitilire Atate
Mundikumbukire Atate
Mafuna ntayiphula nane
Mene mudalitsa enawa
Musandipitilire Atate
Chaka chino chokha ndifuna ndiyiphule
Chaka chino chokha ndifuna ndiyiphule
Zokhumba za mtima wanga ndigule
Zokhumba za mtima wanga ndigule
Chaka chino chokha ndifuna ndiyiphule
Chaka chino chokha ndifuna ndiyiphule
Zokhumba za mtima wanga ndigule
Zokhumba za mtima wanga ndigule
Ambuye oneni, oneni
Ndinu nokha odalitsa tandioneni
Ambuye oneni, oneni
Ndinu nokha odalitsa tandioneni
Ambuye oneni, oneni
Ndinu nokha odalitsa tandioneni
Ambuye oneni, oneni
Ndinu nokha odalitsa tandioneni
Andione
Ambuye oneni, oneni
Tandioneni
Talalala
Ndimazifunsa ndikakhala pansi
Amene anayiphulawa anaponda pati?
Ndimazifunsa ndikakhala pansi
Nanga ineyo ndikayesa zimavuta pati?
Daily nanga daily nanga ndizingovutika?
Daily nanga daily nanga ndizingopilira?
Ambuye oneni, oneni
Ndinu nokha odalitsa tandioneni
Ambuye oneni, oneni
Ndinu nokha odalitsa ndi tandioneni
Ambuye oneni, oneni
Ndinu nokha odalitsa tandioneni
Ambuye oneni, oneni
Ndinu nokha odalitsa ndi tandioneni
Chaka chino chokha ndifuna ndiyiphule
Zokhumba za mtima wanga ndigule
Zokhumba za mtima wanga ndigule
Chaka chino chokha ndifuna ndiyiphule
Chaka chino chokha ndifuna ndiyiphule
Zokhumba za mtima wanga ndigule
Zokhumba za mtima wanga ndigule
Written by: Joseph Chintapase
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...