album cover
album cover
Asa은(는) {albumName} 앨범에 수록된 곡으로 2025년 5월 16일일에 Royal Image에서 발매되었습니다.Cifu
앨범Cifu
2025년 5월 16일
라벨Royal Image
BPM92
멜로디에 강한 음악
어쿠스틱 악기 중심
발랑스
춤추기 좋은 음악
에너지

뮤직 비디오

뮤직 비디오

가사

(Sa-Sa-Sa-Sa)
(Savage, Savage, Savage)
(Njuchi)
Mantha amachoka anawa, akamandiona
Amadziwa pali soja anawa, akamandiona
Khumbo langa apapa
Ndipempha mundichize
Kuti chonde ana angawa
(Asa) asadziwe
Ma injury a soja
Ma injury a soja awa (asadziwe)
Zoti pena ndimalema
Zamabala amu mtima awa (asadziwe)
Ma injury a soja
Ma injury a soja awa (asadziwe)
Zoti pena ndimatopa
Nane ndi munthu ndimafooka awa (asadziwe)
Asadziwe (asadziwe)
Zomwe ndimawona
Zomwe ndimaona ba (asadziwe)
Asadziwe, eeh (asadziwe)
(Mabala amu mtima, mabala amu mtima awa, asadziwe)
Asadziwe ndimadutsa mu zikhomo
Bread ndimawinira zisomo
Ndikafika nkulandilidwa pa khomo
Ndimangoti Ambuye zikomo
I sacrificed my nights for them to see a brighter day
I now fight my fights just to see dem smile at me (oh-oh)
Ma injury a soja
Ma injury a soja awa (aah)
Pena ndimalema koma ndimangozisunga mu mtima (oh)
Ma injury a soja
Ma injury a soja awa (aah)
Asadziwe onsewa Jah
(Asadziwe onsewa Jah aah)
Asadziwe, asadziwe
Zomwe ndimawona, zomwe ndimaona Baba (asadziwe)
Asadziwe, eeh (asadziwe)
(Mabala amu mtima, mabala amu mtima awa, asadziwe)
Koma the way how we do it Jah
Samadziwa amangowona zachitika
Timavaya through sweat before sweeter
Filimu ndi yanga koma si akita
Samadziwa ndimvera ine
Nkona akusangalala nzomwe ndifuna ine
Nkhondoyi sindingawalore kuti ajoine (shh)
(Ma injury a soja)
(Ma injury a soja, ma injury a soja)
(Oooh, yeah)
(yeah, yeah)
(Njuchi)
Written by: Chifuniro Magalasi, Chikondi Mungwa, GIFT SALIKA
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...