album cover
Wekha
album cover
Wekha은(는) {albumName} 앨범에 수록된 곡으로 2025년 5월 16일일에 Royal Image에서 발매되었습니다.Cifu
앨범Cifu
2025년 5월 16일
라벨Royal Image
BPM80
멜로디에 강한 음악
어쿠스틱 악기 중심
발랑스
춤추기 좋은 음악
에너지

뮤직 비디오

뮤직 비디오

가사

Zonse amadziwa
Inde sungabise
Moyo unawudziwa
Unawudziwa uli mwana
Yesu samagona
Yesu samagona pa ana ake
Zonse amaona
Zonse amaona
Wachoka khomo la usiwa
Wakula moyo wawumasiye
Mavuto unawadziwa
Unawadziwa uli mwana
Yahweh samagona
Yahweh samagona pa ana ake
Zonse amaona
Zonse amaona
Wekha, wekha, wekha
Mvera suli wekha
Wekha, wekha, wekha
Sangakusiye wekha
Yesu samagona
Samagona pa ana ake
Mbuye samagona
Samagona pa ana ake
Mmh!
Allah samagona
Allah samagona
Amadziwa pena
Umakhetsa misozi pena
Chikondi suchidziwa
Chomwe umadziwa ndi ululu
Allah samagona
Zonse amaona
Sachedwa, safulumira
Zonse amakonza munthawi yake
Ooh, amadziwa pena
Umafika potopa pena
Moyo ngati uli m'gahena
Kuti ungodzikhweza pena
Allah samagona
Zonse amaona
Sachedwa, safulumira
Zonse amakonza munthawi yake
Wekha, wekha, wekha
Mvera suli wekha
Wekha, wekha, wekha
Sangakusiye wekha
Yesu samagona
Samagona pa ana ake
Mbuye samagona
Samagona pa ana ake
Mvera suli wekha
Sangakusiye wekha
Samagona pa ana ake
Samagona pa ana ake
Written by: Atikonda, Chifuniro Magalasi, Gunthako
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...