album cover
Katatu
album cover
Katatu은(는) {albumName} 앨범에 수록된 곡으로 2025년 6월 12일일에 Deebo Creatives에서 발매되었습니다.First Born
Released2025년 6월 12일
라벨Deebo Creatives
BPM100
멜로디에 강한 음악
어쿠스틱 악기 중심
발랑스
춤추기 좋은 음악
에너지

가사

Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Dzulo tinali limodzi yeah
Mkumati simungandisiye
Dzulo tinali limodzi yeah
Mkumati simungandithawe
Lelo chikondi chija chasintha
Malonjezo aja apita
Mwaonetsa kale mbendela yofiila
Pamalo sipangapa mzipita aaah
Oyamba sineyo (kukanidwa kukanidwa)
Oyamba siine yiii iyee (kusiidwa kusiidwa)
Mkachitatu, mkachitatu, mkachitatu uuuu ooo!
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Akakwela Benz samafuna kutsika
Abwenzi anga mwayamba matama
Dzana lomweli mumati mandifila
Mwapeza wina lelo mwandikana
Ooh I'm such a fool, for you
Donayi yandipha nzeru
Don't know what to do, I'm confused
Harriet wandipha nzeru
Aka sikoyamba wandikana katatu
Wandinyoza pagulu
So I'm moving on tonight
Cause I read between the lines oh aaa!
Oyamba sineyo (kukanidwa kukanidwa)
Oyamba siine yiii iyee (kusiidwa kusiidwa)
Mkachitatu, mkachitatu, mkachitatu uuuu ooh
Oyamba sineyo (kukanidwa kukanidwa)
Oyamba siine yiii iyee (kusiidwa kusiidwa)
Mkachitatu, mkachitatu, mkachitatu uuuu ooo
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Mwandikana katatu
Written by: Emily Zintambira
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...