album cover
Anthu
60
Afro-Beat
Anthu은(는) {albumName} 앨범에 수록된 곡으로 2025년 11월 13일일에 7433591 Records DK에서 발매되었습니다.CHOSEN
album cover
앨범CHOSEN
발매일2025년 11월 13일
라벨7433591 Records DK
언어English
멜로디에 강한 음악
어쿠스틱 악기 중심
발랑스
춤추기 좋은 음악
에너지
BPM100

크레딧

작곡 및 작사
Prince chitz
Prince chitz
작사가 겸 작곡가
Chawanagwa Ngoma
Chawanagwa Ngoma
작사가 겸 작곡가
프로덕션 및 엔지니어링
Chawabeats
Chawabeats
프로듀서

가사

Jagga
Mmh Jagga
Prince mmh Jagga
Zatheka bwa
Kuswela mtima dolo ngati ine zomwe ndili nazo
Zavuta bwa
Ndaziwano kuti siiona nkhope heartbreak
Ndachilapa
Kuswela mtima dolo ngati ine zomwe ndili nazo
Zavuta bwa
Ndaziwano kuti siiona nkhope heartbreak
M'mene ndakongolela inemu
( anthu mulibe chisoni)
Zoona kundiswela mtima ine koma hmm mmh
Anthu ndioyipa awa
M'mene ndimatchenela inemu
( anthu mulibe chisoni)
Zoona kundiswela mtima ine koma hmm mmh
Anthu ndioyipa awa
For sure for sure
Mpaka kuswela mtima msilikali ati akuombele iwe
For sure for sure
Mpaka kuswela mtima chigigo simuopa Kupondedwa
Mbili munaononga kale anthu oyipa inuyo
Zoti ndiwa asthma simuona
Olo zoti kwathu munafika kale sizikukhuzani inuyo
No feeling pity inuyo
Mulibe mantha inuyo
Wamasiye kale ine
( kundisiya choncho)
Wama dimples ine
( mpaka kundisiya choncho)
Duntuntu ine
Hmm waaa khunyu ine
( mpaka kundisiya choncho)
M'mene ndakongolela inemu
( anthu mulibe chisoni)
Zoona kundiswela mtima ine koma hmm mmh
Anthu ndioyipa awa
M'mene ndimatchenela inemu
( anthu mulibe chisoni)
Zoona kundiswela mtima ine koma hmm mmh
Anthu ndioyipa awa
Mpaka kuswela mtima doctor
Kunamiza wa polisi mpaka ku gonja
Politician wandaleyu sakuopsani
Kuwatchita abusa azaku otchani
Ambuye akuoneni
Kusiya mfana opusha hustle ( waluza ndiwe)
Kundisiya poti ndima Beta ( waluza)
Kasiye mfana oyendela paso ( waluza ndiwe)
Kusiya mfana ogeza ( waluza)
Wamasiye kale ine
( kundisiya choncho)
Wama dimples ine
( mpaka kundisiya choncho)
Duntuntu ine
Hmm waaa khunyu ine
( mpaka kundisiya choncho)
M'mene ndakongolela inemu
( anthu mulibe chisoni)
Zoona kundiswela mtima ine koma hmm mmh
Anthu ndioyipa awa
M'mene ndimatchenela inemu
( anthu mulibe chisoni)
Zoona kundiswela mtima ine koma hmm mmh
Anthu ndioyipa awa
Written by: Chawanagwa Ngoma, Mwabi Prince Chitedze
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...