album cover
Ex
album cover
Ex은(는) {albumName} 앨범에 수록된 곡으로 2026년 6월 12일일에 It's Only Entertainment에서 발매되었습니다.Mphungu
앨범Mphungu
2026년 6월 12일
라벨It's Only Entertainment
언어English
BPM100
멜로디에 강한 음악
어쿠스틱 악기 중심
발랑스
춤추기 좋은 음악
에너지

가사

Sameface on the beat
Chikomekome cha
Chikomekome cha
Ndishauwe
Ndishauwe (Yeah)
(Mphungu screeching)
Very Good Very Good
Samafuna kuonjezera body count
Akumabwerabe ex
Mesa mumati ineyo I'm down and out
Koma mwabelanso ex
Mesa mumati wa nyowaniyi amandiposa
Samakupatsa makwacha koma zi ma USA
Galimoto yake ndi chi beast cholusa
Aliyense amamtembenukira akadutsa
Pano ukunena kuti you miss my strokes
Ukuti ndimatha zintchito za grown folks
Ife timapanga zimenezi no jokes
Timadya katundu ndi pakamwa no forks
Chikomekome cha Ex
Chikomekome cha Ex
Amafunabe ndishauwe
Amafunabe ndishauwe (Yeah)
Chikomekome cha Ex
Chikomekome cha Ex
Amafunabe ndishauwe
Amafunabe ndishauwe (Yeah)
Shala kamdau (Baby)
Shala kamdau (Baby)
Baby ndishauwe
Baby ndishauwe
Baby ndishauwe
Samafuna kuonjezera body count
Bestie ndi ex
Amadziwa kuti Atigo is very endowed
Samatalikila ex
Mesa munafikapo mpaka pomandinyoza
Kumandinamizira kuti ndimakuzunza
Kuti umakhalira zipatala ku ma Tunza
Ndipo sindimakukonda ndimakuuser
Pano mwabwera ku sleepover
Kuchotsa matsireku Kodi love hangover?
Ine ngati ashawo pa Hannover?
Apa pokha ndalimba mtima it's over
Chikomekome cha Ex
Chikomekome cha Ex
Amafunabe ndishauwe
Amafunabe ndishauwe (Yeah)
Chikomekome cha Ex
Chikomekome cha Ex
Amafunabe ndishauwe
Amafunabe ndishauwe (Yeah)
Shala kamdau (Baby)
Shala kamdau (Baby)
Baby ndishauwe
Baby ndishauwe
Baby ndishauwe
Written by: Noel Phyzix Chikoleka
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...