album cover
Dolo
album cover
Dolo은(는) {albumName} 앨범에 수록된 곡으로 2026년 6월 12일일에 It's Only Entertainment에서 발매되었습니다.Mphungu
앨범Mphungu
2026년 6월 12일
라벨It's Only Entertainment
언어English
BPM95
멜로디에 강한 음악
어쿠스틱 악기 중심
발랑스
춤추기 좋은 음악
에너지

뮤직 비디오

뮤직 비디오

가사

Matukutuku eti
Ineyo sindikuyenera kukhala ndi matukutuku
Koma pano ndikuuzeni
Ineyo ndi dolo
Hehihihihihi
Kumeneko sindikuzikweza
Ineyo guys
Olo inuyo Mukudziwa kuti mfana uyuyu ndi dolo
Alright guys you've been here with me
Hahahahahahaha
(Mphungu screeching)
Dolo
Dolo ine
Yeah
Very Good Very Good
Dolo ine
Yeah
Yeah
Tonicity
Chinochi nde chinochi very timeless sichilemekeza watch
Chimaunikila njira ngati ndi chi torch
Mafana amafuna chitagwa koma chimaima nji
Am a pyramid ana onsewa ndi mame
Nyimbo zawo zambiri m'zoti awatame
I'm on life-long mission to teach the kids
That's why nyimbo zanga zambiri sindinaname
Zoti ine ndine dolo is an understatement
Ineyo ndine dolo wa madolo that's the statement y'all
Super independent not dependent y'all
Ndimadyetsa family yanga ine nde udolowo
Dolo Dolo Dolo Dolo Dolo Dolo ine
Dolo Dolo Dolo Dolo Dolo ine
Ndine Do Ndine Do Ndine DoDoDoDoDoo
Ndine Do Ndine Do Ndine DoDoDoDoDoo
Ndinachoka 2far ndili kapolo bro
Olo ka VW kongoyendera ka Polo ka bho
Ndinayenda ndekha kuchoka ku too far
Osatenga shortcut ndinafika bhobho
Ndilibe deal yochapa dollar dollar zili mu khola
Amabwera sindilora moyo wanga I'm the controller
Samandionera kukondwa koma madolo
Pakali panopo town inadzadza ndi madolo
Ena osafika folo ena a folo ena oyidutsa folo
Koma onse ndi madolo
Over here we praying for a better tomorrow
When time is gone it's gone you can never go borrow
Dolo Dolo Dolo Dolo Dolo Dolo ine
Dolo Dolo Dolo Dolo Dolo ine
Ndine Do Ndine Do Ndine DoDoDoDoDoo
Ndine Do Ndine Do Ndine DoDoDoDoDoo
Dolo Dolo Dolo Dolo Dolo Dolo ine
Dolo Dolo Dolo Dolo Dolo ine
Ndine Do Ndine Do Ndine DoDoDoDoDoo
Ndine Do Ndine Do Ndine DoDoDoDoDoo
Ah ineyo
Ah ah ineyo ndi dolo
Hahahahahahaha
Ngini ngini ndimaitsata
You know ndimaitsata ngini
Ineyo you can give me china chilichonse chachilendo
Nditha kuchita transform chiyenda
Ngini ndimaitsata
You know it's a blessing I know kuti God gave me
But if people would hate me for that
They should go to hell
They should got to hell
Written by: Noel Phyzix Chikoleka
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...