album cover
M'bale
album cover
M'bale은(는) {albumName} 앨범에 수록된 곡으로 2026년 6월 25일일에 13056262 Records DK에서 발매되었습니다.M'bale - Single
발매일2026년 6월 25일
라벨13056262 Records DK
언어English
BPM97
멜로디에 강한 음악
어쿠스틱 악기 중심
발랑스
춤추기 좋은 음악
에너지

뮤직 비디오

뮤직 비디오

가사

Mbale weni weni wokhala limozi
_Pomwe ukusalidwa
Ichi n'chifuka chake tilibe limozi
_Olo utamangidwa
I know zingavute bwanji tikhala limodzi
_Pamene wafeledwa
Relo kusemphana chichewa mawanso limodzi
_Olo wachepekedwa
M'bale weni weni wokhala limdzi
No matter mukumane jonzi
Mbale weni weni wokhala limodzi
Pazonse kukhala limodzi
M'bale azikhala pa ndalama
M'bale azikhala pa mavuto
M'bale azikhala pakulila
M'bale azikhala pakuseka
M'bale ndi m'bale phanthiphanthi
M'bale ndi m'bale phanthi phanthi
M'bale ndi m'bale phanthi phanthi
M'bale ndi m'bale phanthi phanthi
M'bale ndi m'bale phanthi phanthi
M'bale ndi m'bale phanthi phanthi
M'bale ndi m'bale phanthi phanthi
M'bale ndi m'bale
M'bale weni weni wokhala limodzi
_Kumasukilana zikachitika
Nthawi zomse kukhala limodzi
_Kumawuzana nkhani zakukhosi
M'bale weni weni wokhala limodzi
_Kwinaku mukusungilana zinsisi
Nthawi zomse kukhala limodzi
_Nyengo yotentha ndiyozizila
M'bale weni weni wokhala limodzi
No matter mukumane jonzi
Mbale weni weni wokhala limodzi
Pazonse kukhala limodzi
M'bale azikhala pa ndalama
M'bale azikhala pa mavuto
M'bale azikhala pakulila
M'bale azikhala pakuseka
M'bale ndi m'bale phanthiphanthi
M'bale ndi m'bale phanthi phanthi
M'bale ndi m'bale phanthi phanthi
M'bale ndi m'bale phanthi phanthi
M'bale ndi m'bale phanthi phanthi
M'bale ndi m'bale phanthi phanthi
M'bale ndi m'bale phanthi phanthi
M'bale ndi m'bale
Written by: Man Chi Chiwambo

Loading...