album cover
Timamva
album cover
Timamva은(는) {albumName} 앨범에 수록된 곡으로 2025년 7월 25일일에 Manifest에서 발매되었습니다.Twenty Somethxngs
2025년 7월 25일
라벨Manifest
언어English
BPM119
멜로디에 강한 음악
어쿠스틱 악기 중심
발랑스
춤추기 좋은 음악
에너지

뮤직 비디오

뮤직 비디오

가사

I just try my best
Ndimakankha
And I’m not where
Nnali dzana
Tachoka ndikutali
I’ve seen my family be blessed
I know times really change
Koma tinamva
Ankatikamba
Ankatinena
Ati simudzafika apa
Ife tinamva
Timamva
Timamva
Tima
Mumatinena
Kuti Sitibwela
Lero tabwela
Mumva m’bebe
Mumatinena
Kuti Sitibwela
Lero tabwela
Inu Mumva m’bebe
Oh mumva m’bebe
M’bebe
Inu Mumva m’bebe
Inu Mumva m’bebe
Ndinali nalo tsogolo langa
Koma Akulu anati kagone mwana
You’re too young to have a dream in mind
Analikana tsogolo langa
Koma sinamvele
Lero zili better
Ngakhale malire aja anatiyikila tinawadusa
Now I know the way
Ngakhale ndili ndekha
Zoti tidzafika apa samamvetsesa
Tinawadutsa
Mumatinena
Kuti Sitibwela
Lero tabwela
Mumva m’bebe
Mumatinena
Kuti Sitibwela
Lero tabwela
Inu Mumva m’bebe
Oh mumva m’bebe
M’bebe
Inu Mumva m’bebe
Inu Mumva m’bebe
Written by: Praise Umali, Shafie Phiri
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...